WIZ SPARK INKOS

WIZ SPARK INKOS Wiz Spark
Artist
Afrodancehall
Hip Hop
Mountain Top Muzk
Musician Band
WahYase Boss

28/07/2025

DPP√

25/07/2025



Chipani cha National Democratic Party (NDP) chomwe mtsogoleri wake ndi a Frank Mwenifumbo chalengeza kuti chalowa mu mgwirizano ndi chipani cha DPP.

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi a Chikondi Mpokosa atsimikiza za izi ponena kuti zipani ziwirizi zinali ndi zokambirana masana mpaka usiku wa dzulo.

A Mpokosa ati kutsatira mgwirizanowu, a Mwenifumbo omwe anapereka kale K10 million potenga ma pepala owonetsa chidwi kuimira mpando wa president, saimira nawo pa chisankho cha chaka chino ndipo atsatira a Peter Mutharika.

A Mwenifumbo amafunika kukapereka zikalata zawo lero masana koma malinga ndi a Mpokosa izi sizichitikanso kutsatira mgwirizanowu.

Wolemba WIZ SPARK INKOS

Inkosi 😎
22/07/2025

Inkosi 😎

Kuzipeza Kuzimwela Basi K.K
01/07/2025

Kuzipeza Kuzimwela Basi K.K

25/06/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! HASTINGS HEPPEN, Jixyra Mw Officialfans

Get And Listen my Songs Via Audiomack Now
21/06/2025

Get And Listen my Songs Via Audiomack Now

Stream MOZAYA x WIZ SPARK-BASI.Prod song from WIZ SPARK-BASI.Prod. Featuring: MOZAYA Album: single. Release Date: June 21, 2025.

Awa nde Ndi Panjatu😂😂😂
19/06/2025

Awa nde Ndi Panjatu😂😂😂

12/06/2025

I need Zambian Upcoming Artist ngt ulipo Come ku Inbox timvane

11/06/2025

Anemwe Black Nina I Need Yo Help 🙏

Address

Mulanje

Telephone

+265993347515

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when WIZ SPARK INKOS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to WIZ SPARK INKOS:

Share