Nyasa Network

Nyasa Network Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nyasa Network, Digital creator, Mzuzu.

~Job vacancy sharing
~CV writing and editing
~Application & Resignation sample letters
sharing
~Interview tips sharing
~Business advertisements
~Worldwide News sharing
**Your Only Trusted Source**
:
0896009649
(WhatsApp Only)

30/06/2025

Hie Fam

28/05/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Nelly MD Mzumala, Scalper G Nkhata

Former President wa ku USA, Joe Biden amupanga diagnose ndi prostrate cancer.Nthawi zambiri, prostrate cancer imapandidw...
19/05/2025

Former President wa ku USA, Joe Biden amupanga diagnose ndi prostrate cancer.

Nthawi zambiri, prostrate cancer imapandidwa treat bwinobwino akayipeza msanga.

Prostate ndi chiwalo chomwe chimakhala mkati, cholumikizana ndi katundu wa azibambo.

Koma ya Biden ayipeza mochedwelapo moti yapitilila nkufika pa fupa. Akuti ndi ya aggressive.

Anthu ambiri kuphatikiza President Trump atumiza mafuno abwino.


Azibambo akafika dzaka 40 amayenera kumayezetsa prostate cancer chaka chilichonse. Izi zimathandiza kuti matendawa ngati alipo, apezeke msanga ndipo treatment iyende bwino.

Tipangeni Follow pogwiritsa ntchito link iyi:https://www.facebook.com/profile.php?id=100089986216054

NKHANI MWACHIDUREChris Brown pano wakanizidwa belo ndipo adakasungidwabe ku Danjoni za ndende zaku UK ndipo ali pa  chio...
19/05/2025

NKHANI MWACHIDURE

Chris Brown pano wakanizidwa belo ndipo adakasungidwabe ku Danjoni za ndende zaku UK ndipo ali pa chiopsezo chokhalabe kundendeko kwa myezi iwiri mpaka isanu. Chodabwitsa kwambiri n’chakuti ma concert ake onse agulitsidwa kale ndipo ayamba pa June 13.

Zonsezi zachitika chifukwa cha nkhondo yomwe inachitika zaka ziwiri zapitazo. Wovulazidwayo akunena kuti anavulala kwambiri moti samatha kupita ku ntchito kwake kwa ka nthawi zomwe zinamupangitsa kuluza ntchitoyo yomwe ankalandira $300,000 pa mwezi. Tsopano Chris akuyembekezeka kulipira ndalama zoposa $2 miliyoni ngati chipukuta misozi.

Chris Brown wagulitsa ma concert omse ( sold out) ama stadium atatu ku UK a ndalama zoposa $10 miliyoni, koma tsopano akhoza kukakamizidwa kubweza zonsezo.

Phunziro lofunika: phumzirani kuugwira mtima komaso kulamulira mkwiyo wanu.

khalani pomwepo kuti musamaphonyane ndi mkhani zikuluzikulu zochitika mdziko muno komaso maiko akunja.

Follow Us Using The Link:https://www.facebook.com/profile.php?id=100089986216054

17/05/2025

VACANCY ANNOUNCEMENT AT MALAWI POSTS CORPORATION

POSITION: COURIER LOADERS

Location: Lilongwe and Chichiri

JOB DESCRIPTION
An opportunity has arisen at Malawi Posts Corporation to fill the following vacancy:

Position: Courier Loader

Grade: M12

REQUIREMENT:
- MSCE.

DUTIES AND RESPONSIBILITIES
Loading and offloading of courier shipments.
Collecting and delivering courier shipments to Corporate and individual
customers.
Ensuring that courier shipments are well balanced at the collection point.
Ensuring that all fragile shipments are well loaded.
Ensuring all shipments are properly weighed
Assisting in the general cleaning of courier premises and offices.
Assisting in loading truck loads for customers' shipments
Accompanying the truck on the trunk route.
Any other related duties that may be assigned by his superior from time to time.

MODE OF APPLICATION
Applications with a curriculum vitae and copies of certificates must be sent to:

Deputy Director Admin & HR
Malawi Posts Corporation
P.O Box 602
BLANTYRE.

The closing date for receiving of applications is 26th May, 2025. Only shortlisted candidates will be contacted for interviews.

Follow Nyasa Network for more job vacancies: https://www.facebook.com/profile.php?id=100089986216054

17/05/2025

VACANCY ANNOUNCEMENT@ ESCOM LIMITED

POSITION: TEMPORARY OFFICE ASSISTANT

Location: Distribution South

JOB DESCRIPTION
The Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) Limited is inviting applications from suitably qualified candidates for the position of Temporary Office Assistant (ES 14) for a period of 6 months at the Distribution Offices – South.

Reporting to: Administrative Officer

Location: Distribution South

Key Duties and Responsibilities:

Cleaning the offices

Delivering mails

Performing any other duties assigned from time to time

Minimum Qualifications and Experience:

Malawi School Certificate of Education (MSCE)

Must be physically fit and sober-minded

Must have no criminal record

Application Details:

Interested candidates should submit their application letters together with:

A detailed Curriculum Vitae (CV)

Copies of certificates

Three (3) traceable references

Deadline for applications: 26 May 2025

Submit to:

The Human Resources Office
Chichiri Power Station
P.O. Box 2047
BLANTYRE

Follow Nyasa Network for more job vacancies: https://www.facebook.com/profile.php?id=100089986216054

Click this link to follow Malawi Job Vacancies WhatsApp channel
https://whatsapp.com/channel/0029VaeEdz5B4hdXFDsiE30M

Email: [email protected]

WhatsApp +265880813413

ARRESTED FOR ARMED ROBBERY AND MURDER  Police in Mzuzu have on 13 May, 2025, arrested Elia Levison, Jimmy Nyirenda, and ...
14/05/2025

ARRESTED FOR ARMED ROBBERY AND MURDER


Police in Mzuzu have on 13 May, 2025, arrested Elia Levison, Jimmy Nyirenda, and Jimmy Adam for armed robbery and murder after investigations linked them to several violent crimes in the city.

According to Mzuzu Police Deputy Public Relations Officer Sub Inspector Cecilia Mfune, the first suspect was arrested in Katoto, leading to the capture of two others in Sozibele Lines. Another suspect, Patrick Phiri, was shot dead after pointing a loaded pistol at police officers during the raid.

Mfune says the group robbed Andrew Katona of K5 million and a Samsung phone in Luwinga Township on May 10, 2025, firing three shots into the air before escaping.

The suspects confessed to stealing K100 million from businessman Hassim Irfan on April 24, 2025, and are linked to the murder of Chiukepo Sichali, who was killed on March 27, 2025.

Police recovered a blue Toyota Vitz, a pistol, 58 bullets, two mattresses, a home theatre, a 42-inch TV, and 40 bags of cement. The suspects will appear in court soon to face murder and robbery charges.

(by Towera Katswiri-Mzuzu: 05/14/25)

AMANGIDWA CHIFUKWA CHOGWILILIRA Apolisi ku Chitipi mu mzinda wa Lilongwe amanga abambo awiri kamba kowaganizira kuti agw...
14/05/2025

AMANGIDWA CHIFUKWA CHOGWILILIRA


Apolisi ku Chitipi mu mzinda wa Lilongwe amanga abambo awiri kamba kowaganizira kuti agwililira mayi wina wazaka 25.

Malingana ndi mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu, abambowa ndi a Gedeon Samuel azaka 20, a Steve Robert a zaka 22 komanso bambo wina yemwe apolisi akumusakabe.

Iwo ati izi zinachitika lamulungu chama 8 koloko madzulo pomwe mayiyu amachoka pa golosale ina kukagula zinthu. Abambo atatuwa akuti anamugwira mayiyu ndi kumukokera ku chinyumba chosatha.

A Chigalu ati kumeneko, abambowa analandizana kugwililira mayiyu. Mayiyu atapita ku polisi anamutengera kuchipatala komwe madotolo akatsimikiza kuti anagwililidwadi.

Apolisi amanga abambo awiriwa potsatira kafukufuku wawo, ndipo abambowa awuza apolisi kuti anachita izi chifukwa cha mowa.

(by InnocentKumchedwa-Lilongwe;05/14/25)

13/05/2025
13/05/2025

CHIZONONO

∆ Chizonono ndi nthenda yomwe imayambitsidwa ndi ma bacteria 🦠 kwambiri imafala kamba kogonana mosaziteteza ndi Munthu amene ali ndi nthendayi. Ikalekeleledwa imayambitsa mavuto aakulu pa Moyo wa Munthu.

ZIZINDIKIRO

AMUNA
•ululu pokodza zosakanikirana ndi umuna
•kutupa kwa batire limodzi
•kuyabwa

AKAZI
•kutuluka chikazi mosakanikirana ndi mikodzo kumva kuwawa pokoza
•kutuluka magazi pogonana komanso period yosakhala bwino
•mmimba kupweteka
•chiuno kupweteka.
•Kutulusa fundo lonunkha kwambiri ku Ndata

Chizonono chimankhudza malo ena mnthupi mwa tonse monga

RE**UM: MODUTSA CHIMBUDZI

•kuyabwa kobibira
•kuoneka madontho amagazi mubibi komanso umantchima kwambiri kuti zitheke.

MMASO
•mmaso amawawa
•amadana mkuwala
•amatuluka manthongo

PAKHOSI
•zilonda mkati mwanjira ya zakudya
•kutupa kumaona ngati uli ndi mathonsozi

M'MA JOINTS
•umakhala ndi madzi oipa mmaondo
•mabondo amatentha, kutupa, kuwawa, umavutika kuyenda chifukwa cha ululu.

ZOYAMBITSA
•tikati chindoko chimayamba ndi bakiteliya ndiponso chizonono chimayamba ndi bakiteliya sikuti mabakiteliya amafanana ayi
•bakiteliya ya chindoko ndi "TREPONEMA PALLIDUM"
•bakiteliya ya chidzonono ndi "NEISSERIA GONORRHOEAE"
•chizonono timapatsirana kudzera mukugonana
•kugonana mkamwa
• mathanyula
•kugonana kwenikweniku
•kachilombo ka chidzonono udindo wake waukulu ndi kuyamwa umuna, ndikuononga campany yaubereki kumabatire.

Zoyenera kuchita
•kugonana ndi ambiri
•kupanga mathanyula
•kugonana mkamwa
Izizi mzolakwika chifukwa chizonono chimakhala paliponse mnthupi la odwala

Wapulumuka Pangozi Koma Galimoto Yaphwanyika Chotere— Rodwell Lumbe ndi anzake ena apulumuka pangozi yomwe yachitika ku ...
13/05/2025

Wapulumuka Pangozi Koma Galimoto Yaphwanyika Chotere— Rodwell Lumbe ndi anzake ena apulumuka pangozi yomwe yachitika ku Blantyre mseu wa Magalasi . Ma report akuti anthuwa angovulala pang’ono mosadetsa nkhawa koma kasese yemwe anakwerayo ndiyemwe waonongeka kwambiri. God is good!

Address

Mzuzu

Telephone

+265991695353

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasa Network posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nyasa Network:

Share