Uwona Kuti Upanga Bwanji

Uwona Kuti Upanga Bwanji Uwona Kuti Upanga Bwanji 😊

06/08/2026

Munthu wa Edzi
mupakana kupatuka galimoto panseu!!! anthu inu ma ARV amakukomelani eti...
😫😫😫

Uwona Kuti Upanga Bwanji 😌
06/08/2026

Uwona Kuti Upanga Bwanji 😌

Show ya Gwamba inayenda bwino ndipo takolora 😎
02/08/2026

Show ya Gwamba inayenda bwino ndipo takolora 😎

31/07/2026

Tilimunyengo yangongole mesa πŸ˜‚

30/07/2026

Zikumandiwawa
ndikamawona anthu amene simuna bayitse katemera wa Corona mukadali moyo 😎

30/07/2026

Wakabazayemwe
waombana ndi galimoto ya anduna ku ntcheu, wamwalira atafika nayo kuchipatala πŸ’”
R.I.PπŸ™

Apolisi ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre amanga anthu atatu, a Benson Matiya, Matthews Falaston ndi Henry Mapiri anaba nj...
30/07/2026

Apolisi ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre amanga anthu atatu, a Benson Matiya, Matthews Falaston ndi Henry Mapiri anaba njinga ya moto ya a John Kazembe, amene amachita kabaza.

Wofalitsa nkhani za apolisi ku Bangwe, a Sam Kadyole, ati m'modzi mwa oganiziridwawo anapita pa malo a Number 1 ku Bangwe kumene anawapeza a Kazembe kuti awatenge pa njinga yawo kupita ku mudzi wa Sadiki kokatenga mwana.

Malinga ndi malipoti, oganiziridwa enawo anali atabisala patchire lina kumudziko, ndipo atafika pafupi ndi tchirelo, woganiziridwayo anauza mwini njingayo kuti ayime chifukwa afika. Atayima, anthu awiri aja anatuluka patchirepo atatenga thumba lopanda kanthu ndipo anaveka mwini njingayo kumutu Iwo ndikutenga njingayo kuyamba kuthawa nayo.

Koma mwini njingayo anayamba kukuwa ndipo anthu anakwanitsa kugwira mbavazo ndikuzipangako panel beating pang'ono kenako anayitana apolisi.

Uwona Kuti Upanga Bwanji 😌

Inu ndi mphepoyi mukunena zoona kuti mugona nokha anzanutu aziyambitsa kale 😫😫😫😫
27/07/2026

Inu ndi mphepoyi mukunena zoona kuti mugona nokha anzanutu aziyambitsa kale 😫😫😫😫

THANK YOU SO MUCH Gwamba SHOW IYI SIYIKANABEBA OPANDA INE IWE NDE WAYIWONERA PATALI 🫡πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯🫡
27/07/2026

THANK YOU SO MUCH Gwamba SHOW IYI SIYIKANABEBA OPANDA INE IWE NDE WAYIWONERA PATALI 🫡πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯🫡

27/07/2026

Vuto lake
inuyo zibwezi mukupangira umphawi.......Akangoti ndalama alibe inu basi kumaona ngati samakukondani.😫😫😫

Address

Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uwona Kuti Upanga Bwanji posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share