Mw Daily Update

Mw Daily Update Promote | inform | Entertain.

Koma upcoming artist uyuπŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…πŸ™Œ
01/03/2026

Koma upcoming artist uyuπŸ˜…πŸ˜…πŸ˜…πŸ™Œ

Kuliso uyu Nde a kubwera za hard✊
01/03/2026

Kuliso uyu Nde a kubwera za hard✊

Ndi artist wanji uyuuMutchuleni dzina??
01/03/2026

Ndi artist wanji uyuu
Mutchuleni dzina??

Mwana uja simene kunalili πŸŒ»πŸ’œπŸ™ŒπŸ™ŒEli njuch welcome back
01/03/2026

Mwana uja simene kunalili πŸŒ»πŸ’œπŸ™ŒπŸ™Œ
Eli njuch welcome back

Zikuchitika ndithuEna akut ndiwaku China  anywayWatulusa nyimbo yakeCHRISTAR KYLAπŸ‘‡ Link
17/02/2026

Zikuchitika ndithu
Ena akut ndiwaku China anyway
Watulusa nyimbo yake
CHRISTAR KYLA
πŸ‘‡ Link

Uyu mati ndani omuziwa Inu??
17/02/2026

Uyu mati ndani omuziwa Inu??

Congrats Egie Boy MwPamene walowa mu management ya .All the best 🌻
16/02/2026

Congrats Egie Boy Mw
Pamene walowa mu management ya .
All the best 🌻

Nyamata wapa phalombe watulusa yina kunu
15/02/2026

Nyamata wapa phalombe watulusa yina kunu

Wabeba pa Zambia mwanayuFrom Mzuzu Mpangeni tag ngat mumamuziwa  Us network
15/02/2026

Wabeba pa Zambia mwanayu
From Mzuzu
Mpangeni tag ngat mumamuziwa
Us
network

15/02/2026

Hello everybody.
Pali mwayi kwa upcoming artist oti akhoza kupeza management kumbali ya Audio and videos production.
Njira zake ndi izi πŸ‘‡

1. Tumizani link ya nyimbo yanu ku inbox kwathu.
2. Location yanu komaso kuzilongosola chamba chomwe Inu mukuyimba.
3. Mukasankhidwa muzapasidwa beat kuti muyimbe and osayiwara number phone yanu

Thanks
Follow the page for more information πŸ™

Zikuchitika kuno. Mphatso yomwe wapasidwa ndi chibwez chake ndiyomwe yamukongolesa iye πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™Œ
14/02/2026

Zikuchitika kuno.
Mphatso yomwe wapasidwa ndi chibwez chake ndiyomwe yamukongolesa iye πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™Œ

Address

Mchengautuwa
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mw Daily Update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share