Northern Talented Promo

Northern Talented Promo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Northern Talented Promo, Mchengautuwa, Mzuzu.

Finery Cacoon Vocalist Mw watulusa nyimbo title tiyimbe choir Let's watch it Zabwino kumagawanaNow is out osaiwala kupan...
23/05/2025

Finery Cacoon Vocalist Mw watulusa nyimbo title tiyimbe choir
Let's watch it
Zabwino kumagawana

Now is out osaiwala kupanga subscribe my YouTube channel

Audio Produced by Vplus

Kamwana  aka from mchengautuwa LeonerSky wabwera ndi uthenga kwa day maker wake tiyen timvere nawo k*t akuyakhura zotan ...
29/04/2025

Kamwana aka from mchengautuwa LeonerSky wabwera ndi uthenga kwa day maker wake tiyen timvere nawo k*t akuyakhura zotan wapanga feature woyimba oziwika bwino.

I'm about a da awawatu 🔥❤️
Mix & Mastered by Jacob Hintarh Msango

Hip hop yakumalawi Kod amakumvesan kukoma ndan ?
18/02/2025

Hip hop yakumalawi Kod amakumvesan kukoma ndan ?

Zosayenda from North Nyamata mukumuwona pachithuzi uyo Wamwarira kamba komenyedwa ku  .
06/11/2024

Zosayenda from North
Nyamata mukumuwona pachithuzi uyo Wamwarira kamba komenyedwa ku .

Another one from North Cob Jay Liger this man muli   osati zibwana.Amatha kuyimba  nanji        Dancehall  Amagwetsa mad...
02/11/2024

Another one from North Cob Jay Liger this man muli osati zibwana.
Amatha kuyimba nanji Dancehall Amagwetsa madala madala.

Based at
Artist Wabwino uyu Eeeeee 🙌🙌🙌🙌🙏🙏🙏🙏

Mawu sagonera  Upcoming artist  ndi mwayi wako ozapanga nawo perform   Pa chiwavi  ground
01/11/2024

Mawu sagonera Upcoming artist ndi mwayi wako ozapanga nawo perform Pa chiwavi ground

Macelba 'After The Silence' EP tracklist is out 🎶 1) Munalora2) Olakwa Ndani ?3) Chosadziwa Part 2 ft Leslie4) Ju ft Eli...
30/10/2024

Macelba 'After The Silence' EP tracklist is out 🎶

1) Munalora
2) Olakwa Ndani ?
3) Chosadziwa Part 2 ft Leslie
4) Ju ft Eli Njuchi
5) Chair ft Lipe
6) Stay Winning

Bonus
- Golide ft Janta

The full Ep will be out this Friday !

Mwana waluso uyu From   kupanga thankara ya mafuta yikuyenda
29/10/2024

Mwana waluso uyu
From kupanga thankara ya mafuta yikuyenda

Address

Mchengautuwa
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Northern Talented Promo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share