21/04/2026
Nkhani yachisoni ðŸ˜
Mnyamata mukumuonayi dzina lake ndi Boaz Kambeta, akuti wapezeka lero mamawa ataphedwa kwa Chisinga komwe amakhala ndi mai ake.
Akuti dzulo cham'ma 6 koloko madzulo mayi ake anamutuma mwanayu kuti akatenge phone pa charge kumene anasiya phone-yo kuti awatchajire. Kenako mayi akudabwa mpaka 7 koloko usiku mwana sakubwerabe, kupita kukamufufuza osamupeza. Mamawa wa leroli mwanayu wapezeka ataphedwa phone-yo alibe💔ðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜
Abale tafika mpaka apa? ðŸ˜ðŸ˜ðŸ’”Nkhani yachisoni ðŸ˜
Mnyamata mukumuonayi dzina lake ndi Boaz Kambeta, akuti wapezeka lero mamawa ataphedwa kwa Chisinga komwe amakhala ndi mai ake.
Akuti dzulo cham'ma 6 koloko madzulo mayi ake anamutuma mwanayu kuti akatenge phone pa charge kumene anasiya phone-yo kuti awatchajire. Kenako mayi akudabwa mpaka 7 koloko usiku mwana sakubwerabe, kupita kukamufufuza osamupeza. Mamawa wa leroli mwanayu wapezeka ataphedwa phone-yo alibe💔ðŸ˜ðŸ˜ðŸ˜
Abale tafika mpaka apa? ðŸ˜ðŸ˜ðŸ’”