Uncle Brown Mchantchira

Uncle Brown Mchantchira This is UNCLE BROWN. A radio producer, presenter and music promoter currently working with Umunthu fm

29/10/2025
mawu amodzi kwa Uncle Brown ๐Ÿ˜€
25/10/2025

mawu amodzi kwa Uncle Brown ๐Ÿ˜€

11/10/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Manfred Zalira Betha, Zebron Madalitso, Lameck Chiumia, Jaqueline Chanza, Wiston Elias, Whoosher Hassan Ganizan, Mcdonald Zacharia, Yona Xadreque Timรณteo, Prince Kay Mw, Doctors Ntanga, Steven Wayson, Fรฉlix James, Magombo Mirriam, Gwacha Phiri

31/05/2025

"HSA Riddim"

Ndani wachangu angandikungireko beat ya boh ya dancehall padzina limeneri?

Kozekerani, zisakuphonyeni ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ
17/05/2025

Kozekerani, zisakuphonyeni ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ



Waluso Msabatayi on Umunthu FM

104.4/104.6MHz


Uncle Brown Mchantchira
Kay Krush - Ngweee Music

13/04/2025

Lero 7:00pm ndikhala pa Umunthu FM kucheza ndi Uncle brown (Ernest BJ Mchantchira omwe afunitsitsa kuti acheze nane lero komanso week yamawa Sunday kamba koti Iwo akuti Ali nzambili zoti andifuse.

Program name: waluso msabatayi
Day: every Sunday
Time: 07:00 pm
Host: Uncle Brown Mchantchira
Station: umunthu FM

Lilongwe, mchinji, nkhotakota ndi Madera ozungulira ili pa 104.4 pomwe Ku kasungu and surrounding areas ili pa 104.6

Kwa omwe sitili Madera awa osadanda nditumiza interview ya lero pa Whatsapp channel yanga muivera part one yonse. Komanso interview ikayamba ku comment box ndiika link yoti muvere online

Zuoneka kuti mma radio mu and akutikondatu ma interview ponseponse. ๐Ÿ™Œ

Address

Ntcheu

Telephone

+265998320055

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uncle Brown Mchantchira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category