25/09/2026
Tinapanga post k*t mungathe k*tumiza unthenga uliwonse zithu zomwe zangochitika kumene ku MโDera kwanuko ndi umboni wake, tizapanga post pamudzi pano motsata ndondomeko yathuโฆ
Topfan walira mokweza ku comments box k*t mabwana mwachulutsa chidyerano akazi awo sali safe๐๐๐
Sidenote:
Mabwana chepetsan kadyedwe akukudandaulan๐โ๐ฝ