01/12/2025
Ma sukulu onse aukachanjede mdziko muno kuphatikizapo sukulu ya UNIMA motsogozedwa ndi sukulu ya ukachenjede ya zaulimi ya BUNDA tsopanso abwela poyera nkuvomeleza k*ti sukulu ya ukachenjede ya MZUNI ndiyo tate wa masukulu onse aukachanjede mu dziko muno mu zochitika zambili kuphatikizapo masewero osiyana siyana
Poyankhula ataphopholedwa ngat mavu omanga kuseli kwa poto ophikira komanso atapunthidwa ngat okuba na phone mu nzindq wa limbe inde inu atafafanthidwa ,kusosoledwa ,kupakulidwq ndi kuphulisidwq,matimu a Bunda komanso UNIMA ati tsopano nthawi yakwana k*ti sukulu ya ukachenjede ya MZUNI ilandire ulemu oyenera komanso ilemekezedwe mopitilira Maka pomwe yakhala akatswiri mu masewero osiyana siyana omwe anathandixidwa ndi thumba la ndalama kuchokera ku national bank mu mpikisano wa chaka Chino wa ma sewero osiyana siyana amu sukulu za ukachenjede (2025 national bank TESSAM varsity games)
Kupatulako kupambana mphotho ndi zikho zosiyana siyana kumaloku (UNIMA), mzuni yatsogolanso pakukhala ndi masosobina ooneka bwino komanso Osamba chinthu chomwe mmasukulu aukachenjede ambili Maka ya BUNDA kulibeko
masukulu aukachenjedewa sanabise mawu koma kufotokoza k*ti tsopano iwowo ngat Ana aziitchula MZUNI k*t DADDY π Maka popeleka ulemu uyenera k*ti pasakhale ziwawa
Sukulu ya ukachenjede ya MZUNI ndiyo tate wa ma sukulu a ukachenjede mdziko muno ndipo imaswa kuposa aliyense
Mmene UNIMA imafunsa k*ti chikuchitika ndi chani,MZUNI inali itakang'antha kale zikho zingapo
Wolemba : precious kaunda
GALANTA
Copied