Sir Cossah D

Sir Cossah D You are here for laughing😂, Sir Cossah d is afroDancehall/content creator Entertainment ,,,blackchild straight away from Tengani ghetto empire, Nsanje?

Sir please post me,🙏 ndi funsileni ku gulu zomwe zikundituluka ku masozi mankhwala ndingawapeze bwanji?Nthendayi inayamb...
12/08/2026

Sir please post me,🙏 ndi funsileni ku gulu zomwe zikundituluka ku masozi mankhwala ndingawapeze bwanji?

Nthendayi inayamba tsiku lomwe ndinapita ku hotel ndi chidya makanda china chake ndipo chinandiwuza kuti chindipasa K250000 chomwe amafuna ndichoti andipakule opanda chishango kamba ka umphawi sinachitile mwina ndinavomeleza za offer yomwe anandipasa ija

Ndipo tsikulo abapakuladi nditafika kunyumba ndipo ndinayamba kuwona kusintha kunkhope kwanga sindikutha kunvesa kweni kweni vuto chifukwa kuchipatala ndiye ndapita kambili koma vuto sakulipeza
Please 🙏 kwaomwe akudziwa njila zina ndithandizeni usiku sindikumagona zikumatentha ngat moto

ndatha kunvesa kuti Ng'ona ukaitenga bwino simavuta 🫡
12/08/2026

ndatha kunvesa kuti Ng'ona ukaitenga bwino simavuta 🫡

Mwayimva? Boma la South Africa lalembera boma la Malawi, Nigeria ndi Ethiopia kuti abwezekepo gawo lina la 29 billion kw...
12/08/2026

Mwayimva? Boma la South Africa lalembera boma la Malawi, Nigeria ndi Ethiopia kuti abwezekepo gawo lina la 29 billion kwacha(R292 million) zimene zili ndalama zomwe boma la South Africa lo lidagwiritsa ntchito potumiza nzika za mayikowa mmakwawo.

Ndiye akuti a Malawi pafupifupi 90,000 ndi amene apangidwa deport ku South Africa kuyambira January chaka chino. Ndiye tikapanga masamu apopo, wina aliyense amene anathamangitsidwa ku South Africa akuyenera kubweza K322,222.222 imene ili ndalama yochepa kwambiri kuyerekeza ndi ndalama zimene anthuwa adya kumeneko. Mix “too much money”🤝

koma ma away awa nthawi zina tizawona polekela,, mwina vuto ndiineyo sindikuwonesesa🤔🤔
11/08/2026

koma ma away awa nthawi zina tizawona polekela,, mwina vuto ndiineyo sindikuwonesesa🤔🤔

koma anthu ndie tikupangana nkhanza,, munthu oti amupeza ngakhale anali atalefuka  bwanji sanakwanise kumufusa kuti zina...
11/08/2026

koma anthu ndie tikupangana nkhanza,, munthu oti amupeza ngakhale anali atalefuka bwanji sanakwanise kumufusa kuti zinakhale bwanji, kungofikila kuwotcha nyumba nkuphwanya katundu wamunthu💔🙄

Mbolatu iyi :- Ma galimoto 4, ndi nyumba ya bwana wina zayatsidwa ku Balaka.

Anthu ati awotcha nyumba yo nkuononga katundu ense chifukwa masiku atatu apitayo mayi wina ogulitsa masamba adasowa nde anamupeza pafupi ndi nyumbayo ali ofooka. Basitu anthu angoti atha kukhala adamusunga ndi bwanawo mpaka kuyatsa nyumba yake.

Kodi kukhala kwake tizitele ? Mmmh

apa tipatenge bwino 🫣🫣Pakhoza kuchitika mistake pang'ono🤔🤔
11/08/2026

apa tipatenge bwino 🫣🫣Pakhoza kuchitika mistake pang'ono🤔🤔

kodi sir ndifusileniko ku gulu koma mundibise dzina,,,nditati ndasiya ku user izizi zitha kapena ndigwilise ntchito njil...
11/08/2026

kodi sir ndifusileniko ku gulu koma mundibise dzina,,,

nditati ndasiya ku user izizi zitha kapena ndigwilise ntchito njila yanji,, chifukwa azibambo ayamba kumandikana akumati ndili ndimatenda pamene ayi munthu ine Edzi ndimangoyinvela pa Radio, ndithandizeni mulimonsemo ndinvela💔

abale chifukwa chani anyamata akafika ku Malawi kuno amatsekeka pa kamwa,, anyamata oti timajola nawo ku south Africa pa...
11/08/2026

abale chifukwa chani anyamata akafika ku Malawi kuno amatsekeka pa kamwa,, anyamata oti timajola nawo ku south Africa pano akumangotidusa,, ndie Sir nditseguleniko maso ndikonze pati,,

ine ku Theba nali ndizibwenzi anyamata okha okha koma kuno opanda or m'Modzi kupempha number eti,, kodi timangokongola ku south Africa kokha, thandizeniko chonde mavalidwe achikoka ngati amenewa, mwina ena muzawopa kuganiza kuti tinagwidwa kale koma ayi musawope ndine Osayamba🙄🙄

Player uyuyu mpira amandisewelera bho kwambiri ndisaname. kusamupatsa player of the year nde kulakwatu. moti azimayi aku...
10/08/2026

Player uyuyu mpira amandisewelera bho kwambiri ndisaname. kusamupatsa player of the year nde kulakwatu. moti azimayi akumachita kuposa azibambo maseweledwe awo?

JB. Wayakhula kumbali yake,, imfa zakumalawi pena zimapeleka mantha kwambiri 💔
10/08/2026

JB. Wayakhula kumbali yake,, imfa zakumalawi pena zimapeleka mantha kwambiri 💔

Address

Tengani
4670

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sir Cossah D posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share