Malavi 360 Updates

Malavi 360 Updates A source of verified news
Receive updates on your phone
We also do adverts
Advertise with us contact us on
0887598994

This is the home of verified news

27/09/2024

📌 'sOnFire

  (R) (L)Anyamata awiri ochokera m'sukulu zaukachenjede za University Of Malawi-UNIMA komaso Lilongwe University Of Agri...
27/09/2024


(R)
(L)

Anyamata awiri ochokera m'sukulu zaukachenjede za University Of Malawi-UNIMA komaso Lilongwe University Of Agriculture And Natural Resources-LUARNA apezeka atafa m'sabatayi

Vincent Nyirenda komaso Leonard Buli apezeka atafa kusatira kusowa kwawo mu kapasi za sukulu

Olemba :Fatsan L Robert
(Zomba)

Anthu osawerengeka akhamukila ku mpanda wina mudzi mwa Saidi mfumu yaikulu Msanama m'boma la Machinga komwe kwapezeka ch...
22/08/2024

Anthu osawerengeka akhamukila ku mpanda wina mudzi mwa Saidi mfumu yaikulu Msanama m'boma la Machinga komwe kwapezeka chinthu chodabwitsa ndipo anthu amene afika pa malo-pa akumanong'onezana kuti chinthu-chi ndi ndege ya afiti

James Chisonga popularly known as Jay Jay Cee has today announced his departure from Mabilinganya Empire,a music group w...
22/08/2024

James Chisonga popularly known as Jay Jay Cee has today announced his departure from Mabilinganya Empire,a music group which was formed by the late Matafale

Jay Jay Cee has been a member of Mabilinganya Empire for eleven years

Pamene pangopita tsiku limodzi chichitikileni ngozi ya ndege m'boma la Mkhotakota.Lero pa 22 July 2024 kwachitikaso ngoz...
22/08/2024

Pamene pangopita tsiku limodzi chichitikileni ngozi ya ndege m'boma la Mkhotakota.Lero pa 22 July 2024 kwachitikaso ngozi yoopsa m'boma la Kasungu pa nseu ochoka ku Chinkhoma kupita kwa Msanthe.

Minibus yomwe nambala yake siikudziwika inaombana ndi galimoto yonyamula mafuta pamene amayesayetsa kuzemba was njinga yakapalasa.Tikunenapano minibus-yo yapsa ndipo siikudziwika kuti idanyamula anthu angati koma palibe yemwe wapulumuka

Victory at Bingu National StadiumMaule 3-1 Moyale
21/08/2024

Victory at Bingu National Stadium

Maule 3-1 Moyale

Kwalembedwa kwa munthu kufa kamodziMacelba's dad rest in peace
21/08/2024

Kwalembedwa kwa munthu kufa kamodzi
Macelba's dad rest in peace

Nduna yoona zokopa alendo a Vera Kamtukule atsimikizira kwimbi lomwe adalipedza pa chipatala chachikulu cha Khotakota ku...
21/08/2024

Nduna yoona zokopa alendo a Vera Kamtukule atsimikizira kwimbi lomwe adalipedza pa chipatala chachikulu cha Khotakota kuti boma likhazikitsa kafukufuku pofuna kudziwa chimene chidachititsa kuti ndege yomwe idanyamula anthu atatu paulendo wawo kuchoka ku Khotakota kupita ku Liwonde m'boma la Machinga

Akatukule afika pa chipatala chachikulu cha Khotakota kuzaona mai yemwe wabwelera lokumbakumba atapulumuka pa ngoziyi

Malipoti omwe tikutsatira mwa chidwi akuonetsa kuti yemwe amaongolera ndegeyo anakomoka m'kati mwa ulendo ndipo adakanika kuongolera ndegeyo zimene zidachititsa kuti ndegeyo igwele m'nyanja ya Malawi

Tikhala tikukupasani zambiri pa nkhaniyi

Olemba Fatsan L Robert
Follow us

Minister of information Moses Mkukuyu has confirmed that an aircraft which is owned by Nyasa Express has been involved i...
21/08/2024

Minister of information Moses Mkukuyu has confirmed that an aircraft which is owned by Nyasa Express has been involved in an accident

Address

467 Zomba
Thondwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malavi 360 Updates posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share