Chitemwe Media

  • Home
  • Chitemwe Media

Chitemwe Media Film/Video Production plus News.

16/07/2025
Breaking News Galimoto ya mtundu walole registration BL 7224 yomwe inanyamula chimanga yachita ngozi pa hardware ku Limb...
25/06/2025

Breaking News

Galimoto ya mtundu walole registration BL 7224 yomwe inanyamula chimanga yachita ngozi pa hardware ku Limbe, Blantyre.

Malingana ndi omwe ayandikila pamalopa ati Galimotoyi in yaomba pholo la magesi mmawa cha mma 5 pomwe imafuna kukhota. Sizinaziwike kuti akhuzidwa ndi ngoziiyi ndi angati

Just discussing how powerful the media is, in the Afirnity TV program called"Bwana on the Street". Hosted by Prince Char...
05/05/2025

Just discussing how powerful the media is, in the Afirnity TV program called"Bwana on the Street". Hosted by Prince Charles of Nigeria.

11/03/2025

Malangizo awulele mu nthawi ya Jude ino

Oziwa za nyengo ati pali chiopsyezo choti dziko la Malawi maka mchigawo cha kummwera chikhoza kulandira Mphepo ndi ya mp...
09/03/2025

Oziwa za nyengo ati pali chiopsyezo choti dziko la Malawi maka mchigawo cha kummwera chikhoza kulandira Mphepo ndi ya mphamvu yomwe ingasasule denga za nyumba, kuzetsa mvula yochuluka, kusefukila kwa madzi, kuononga zinthu monga nyumba ndi zina zambiri. Namondweyu yemwe akutchedwa Jude akuyembekezeleka kufika lolemba pa 10 March.

Address


Telephone

+265998192747

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chitemwe Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chitemwe Media:

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share