Mbiri Za M'dziko Lathu - Malawi

  • Home
  • Mbiri Za M'dziko Lathu - Malawi

Mbiri Za M'dziko Lathu - Malawi Telling the young Malawian blood the most interesting stories that happened before their Existance

Malawian Forktales that happened between 1800s-1900s before this generatin

05/08/2025

M'malawi ali ndi mwano ndithu 🤣🤣🤣🤣

28/07/2025

Kodi nzapakanthawi eti???

Some people never change 😊

4 Million Kwacha in the pocket 😊
20/07/2025

4 Million Kwacha in the pocket 😊

PLATFORM FOR INVESTIGATIVE JOURNALISM yatulutsa Report (Including mayina) a anthu anachitira zachipingwe komanso za Upan...
19/07/2025

PLATFORM FOR INVESTIGATIVE JOURNALISM yatulutsa Report (Including mayina) a anthu anachitira zachipingwe komanso za Upandu a Sylvester Namiwa:
Koma achitetedzo athu kuno akuti adakafufuzabe!

Malawi wanga!🤷🏻‍♂️

😊
16/07/2025

😊

06/07/2025

YOU ENDED UP IN A COUNTRY WHERE NONE OF THE CREATURES EXISTING IN THAT COUNTY ARE SERIOUS!

Pathetic!😔

Me looking at Chimwendo Banda leading Chorus in a Church after studying his real character.
01/07/2025

Me looking at Chimwendo Banda leading Chorus in a Church after studying his real character.

THERE SHALL ALWAYS BE SUNSHINE AFTER THE RAINS!😔
01/07/2025

THERE SHALL ALWAYS BE SUNSHINE AFTER THE RAINS!😔

Apa mpanene mungadziwire kuti ku MCP kuja sikuli bwino.Ngati akuthana ndi wawowawo oti akuyendera limodzi, kuli bwanji e...
21/06/2025

Apa mpanene mungadziwire kuti ku MCP kuja sikuli bwino.
Ngati akuthana ndi wawowawo oti akuyendera limodzi, kuli bwanji enawa??🤷🏻‍♂️🤷🏻‍♂️🤷🏻‍♂️🤷🏻‍♂️🤷🏻‍♂️

Mzimu wa Malemu SKC upitilidze kuutsa mu mtendere


A Vitumbiko Mumba alengeza kuti atula pansi udindo ngati membala wa komiti yaikulu ya chipani cha Malawi Congress (MCP).

Iwo awuza Zodiak Online kuti achita izi kaamba ka ndale zothana zomwe anthu ena akhala akuchita m'chipani cha MCP koma iwo adakali membala wa chipanichi.

(by Dickson Chivwati Gondwe-Lilongwe:06/17/25)

21/06/2025

THIS STATEMENT ALONE CAN TELL YOU THAT WE'RE NOT SAFE AND WE'RE NOT IN GOOD HANDS!

OFFICIAL BITTING FELLOW OFFICIAL IN THE SAME PARTY 🤷🏻‍♂️

11/06/2025

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mbiri Za M'dziko Lathu - Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mbiri Za M'dziko Lathu - Malawi:

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share