25/03/2024
Verse Featuring project:
I am happy to announce kuti ndili ndi nyimbo titled yomwe sinatulutse ndipo pofuna kupititsa patsogolo luso la ma upcoming artists azanga ndaganiza zoti ndipange album ya Nyimbo iyi.
Mwina ena simuvetsetsa kuti zotheka bwanji, nalo yankho ndi ili yes ndizotheka and azathu a Kunja there doing this strategy to promote nyimbo zawo. Chomwe chizichitika Muthu akafuna kuti akhale nawo mu album ya ayenera andipeze Ku inbox kapena paliponse pomwe tingakumane and tikakumana ndikupatseni sample ya track yo with a verse ndi hook then mulemba za story yanu kpn yomwe muganiza kuti inamuchitikilako wina then kwinako we proceed.
For more information inbox, we will close akakwana ma track 9. Athu 4 ayimbako kale akhala 5 pangani changu.