Nyasa gossips 265

  • Home
  • Nyasa gossips 265

Nyasa gossips 265 Entertainment gossips and news

With Mackienzie Sebia Makhieza – I just got recognized as one of their top fans! 🎉
13/05/2025

With Mackienzie Sebia Makhieza – I just got recognized as one of their top fans! 🎉

Kodi ku Malawi Gaming and Lottery Authority mukutaniko?Yes...... anthu samachita kukakamizidwa kupita kuma website ko ko...
13/05/2025

Kodi ku Malawi Gaming and Lottery Authority mukutaniko?

Yes...... anthu samachita kukakamizidwa kupita kuma website ko koma umphawi ndi omwe umawapititsako.... advertisement ya ma company mumawalola kubera anthuwa ndi omwe akukopa anthu ambiri... ma stunt a anthu owina akumapanga aja....

check 1. betpawa (Crash games sector) 50 blues in a row.....2 purples (2 or 3 odds) then 70 blues in the row again then 10 odds...then 15 blues in a row then 9.58 odds then....2 odds x 2 then 7 1.00 odds again...is this fair or murder?

2. 888bets... 3 odds seven times then 5 blues then 7 odds then 10 blues then 20 odds the 25 blues..... after 5 rounds of such barbaric gaming experience they come with 9.5 then 8.00 odds then boom 200000 odds after instilling fear in people...... as just to pain a provably fair tag .....

3. Worldstar Betting.... this site has no customer care but cyborgs who doesn't care about people's lives just like the rest of them..... similar patterns but when a player gets lucky to have managed to get some few coins to withdraw.. Withdrawing takes eternity than depositing..... a withdraw can take even up to 7 hours before receiving if you are lucky but mostly they return the funds withdrawn so that you shouldnt come out with any coin......

Betway.......betika,, mmg has no intention of anyone winning anything their strategies are way too much of coning people...

Magla ..... monitor warn and take action on companies that do not let atleast their customers earn something.... dont let people suffer losses of life and after losing too much money.... please....

ANTHU AKUBETSA NDALAMA KU CHINDEGE UKU......

Muli faculty yanji sister?
11/05/2025

Muli faculty yanji sister?

Zosayendatu....ena akatisiya timamva zambiri yawo yabwino koma awawa zikuti bwanji koma? mmmmmh
06/05/2025

Zosayendatu....ena akatisiya timamva zambiri yawo yabwino koma awawa zikuti bwanji koma? mmmmmh

Imfa yovuta kumvetsa mmmh... So Sad
06/05/2025

Imfa yovuta kumvetsa mmmh... So Sad

Anapezedwa akupakula ng'ombe.... aaaa inu ndi stunt iyi...Welcome to Chichiri Prison trailerPhoto Credit: Malawi Voice
05/05/2025

Anapezedwa akupakula ng'ombe.... aaaa inu ndi stunt iyi...Welcome to Chichiri Prison trailer

Photo Credit: Malawi Voice

Bwana Bail sayendera kunseu ......mmmh inu mufune musafune mukathera ku Maula Prison
05/05/2025

Bwana Bail sayendera kunseu ......mmmh inu mufune musafune mukathera ku Maula Prison

chenjezo la ulere.....musabetse account ya facebook mophweka......1. Osalongola link iliyonse yomwe ikubwera pa social m...
05/05/2025

chenjezo la ulere.....musabetse account ya facebook mophweka......

1. Osalongola link iliyonse yomwe ikubwera pa social media mkumanena zogawa ndalama......ndalama sagawana or kungongozana thru facebook or X(Twitter)

2. Osapereka phone number yanu kwa anthu osawadeziwa palibepo chifukwa chomveka

3. Ena ake amabwera ndi ma friend request kenako azikulonjezani ndalama makamaka amabwera ndi ma pictures a akazi ooneka apamwamba...samalani kuli zimphongo zokuba kuseli kwake

4. Ena akunena zoti ku number yanu kwabwera number muwatumizire please osaponya

5. Amuna ena amakonda kunyengelera kuti muwatumizile zithunzi zambulanda please....ichi sichikondi koma utchisi.... Okukonda makulemekeza osati kufunafuna kukuyalutsa....

zikomo kumipando.....follow us and let's grow together

Kodi mumawakumbukila ndi nyimbo zanji madolowa????
05/05/2025

Kodi mumawakumbukila ndi nyimbo zanji madolowa????

anthu mtopolatu uwu.....ena akuti taponyaninso post ija kkkkk mmmh
05/05/2025

anthu mtopolatu uwu.....ena akuti taponyaninso post ija kkkkk mmmh

Kaya walimba mtima kuchimetetsayo ndani? koma ichichi chimatha kukanyanga nsambo  (Acoustic guitar)   mmmm ndiye muli vo...
05/05/2025

Kaya walimba mtima kuchimetetsayo ndani? koma ichichi chimatha kukanyanga nsambo (Acoustic guitar) mmmm ndiye muli voice eeeee chikadzati kodi kuchoka amatere kungochoka osatsanzika ....mmmm mmmh

Eti akuti ma action a big man aakuluwa amafanana ndi President wina wake ku Africa? akuti kumachitidwe.....anthu mtopola...
30/04/2025

Eti akuti ma action a big man aakuluwa amafanana ndi President wina wake ku Africa? akuti kumachitidwe.....anthu mtopola mmmh

Address


Telephone

+265992959714

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasa gossips 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share