Umatha Daily

Umatha Daily Umatha Daily Is Africa’s fastest-growing entertainment brand and a trusted source of reliable news,stories,trends and updates across the continent.
(1032)

For business inquiries,advertising & partnerships:
WhatsApp: +265884715671/+265993926689

10/08/2026

Mulungu Atakupatsani Mwayi Kuti Mupeleke Dzina La Munthu M'modzi Awuke Kwa Kufa Mungakonde Atabwelera Ndani?

Iyi ndi nyimbo imene yapangitsa anthu ambiri kulowa m’mabanja this month.Ngati anthu ambiri akukwatirana, nkhani yake im...
10/08/2026

Iyi ndi nyimbo imene yapangitsa anthu ambiri kulowa m’mabanja this month.

Ngati anthu ambiri akukwatirana, nkhani yake imakhala amvera nyimbo ngati izi, ndipo amakhala akuzimva u Lover Boy ndi u Lover Girl. 👇

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

Bwerani Ticheze Pang’ono.—Uyu ndindani?
10/08/2026

Bwerani Ticheze Pang’ono.

—Uyu ndindani?

10/08/2026

Akazi Ndinu Anthu Achipongwe Komanso Osakhulupilika.

—Oyimba uyu amene dzina lake ndi Scop Dee wayikira umboni atamva nkhani monga yomwe yachitika ku South Africa yowinjirana mkazi oti wangokwatiwa kumene.

Imvani kulira kwa mamuna amene alimu love industry umu 👇
https://youtu.be/OnSUHxWAd4M?si=Wjo5d512SyhtNBwq

10/08/2026

Kwathu si padziko.

Thupi la Malemu Thokozile Machilinga Laikidwa M’manda ku Mzimba.—Thupi la malemu Thokozile Machilinga, yemwe anali wophu...
10/08/2026

Thupi la Malemu Thokozile Machilinga Laikidwa M’manda ku Mzimba.

—Thupi la malemu Thokozile Machilinga, yemwe anali wophunzira wa chaka chachitatu pa Malawi Institute of Journalism (MIJ), laikidwa m’manda lero ku Mzimba.

Machilinga anapezeka atafa ku Naperi, Blantyre, zomwe zasiya chisoni chachikulu pakati pa abale ake, anzake, ophunzira anzake komanso aphunzitsi ake.

Mzimu wake upumule mtendere. 🕊️💔🙏

Thupi La Amene Anali Mkulu Wa MBC Layikidwa M’manda.—Thupi la a Brian Banda layikidwa m’manda masana ano ku Chileka, kum...
10/08/2026

Thupi La Amene Anali Mkulu Wa MBC Layikidwa M’manda.

—Thupi la a Brian Banda layikidwa m’manda masana ano ku Chileka, kumene kunasonkhana anthu ambiri kuti akamupelekeze.

Mzimu wa a Brian Banda upumule mumtendere.

10/08/2026

Prophet Habbakuk Wapereka Uthenga Wopepesa Imfa ya Brian Banda

__Prophet Habbakuk wa Pentecostal Assembly of Malawi wati ndi wokhudzika kwambiri komanso akulira kwambiri pa imfa ya Brian Banda, yomwe yasiya njakata ndi mafunso opanda mayankho anthu ambiri.

Ndipo popitiriza kuyankhula ku likulu la mpingo wawo, ati iwo ndi okhudzika kwambiri, koma poti ndi chikodzera cha Mulungu, momwe anapangira Yudasi pa imfa ya Yesu.

10/08/2026

Amene mukuwatcha Ma Goat Wo Ife Titha Kuwapanga Kanyenya.

—Oyimba awiliwa atha mawu munyimbo yawo ya “Nzika” yi Kaya akuzembera ndani Kaya m***a kupanga find out nokha powonera full video on YouTube.

Santo ft Ably - Nzika
https://youtu.be/MSTUoIfJJek?si=o_Z073JJQyd19KP9

10/08/2026

Bungwe Lama Prophet Onse M'dziko Muno Lapepesa Ndi K100,000 Ku Maliro A Brian Banda.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Umatha Daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Umatha Daily:

Shortcuts

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share