Chinamwali Sounds

Chinamwali Sounds Osaopa πŸ’ͺ osatopa πŸ‹οΈβ€β™‚οΈ osafooka πŸš΄β€β™‚οΈπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

Mfana Oopsa Kwambiri Winiko Spotted at Kakuzu Stadium_Ku Mwambo olumbilitsa Adad..πŸ˜‚πŸ˜‚
04/10/2025

Mfana Oopsa Kwambiri Winiko Spotted at Kakuzu Stadium_Ku Mwambo olumbilitsa Adad..πŸ˜‚πŸ˜‚

Anyamata awiri omwe pakadalipano sakudziwika mayina awo apezeka atafa mamawa uno pafupi ndi malo okwelera minibus zopita...
27/09/2025

Anyamata awiri omwe pakadalipano sakudziwika mayina awo apezeka atafa mamawa uno pafupi ndi malo okwelera minibus zopita mu Limbe omwe ndi oyandikana ndi nyumba za Blantyre Water Board komwe ndi kuseli kwa Kamuzu Stadium.

Anthuwa omwe matupi awo akuoneka ndi zilonda komanso magazi akuganiziridwa kuti achita chophedwa ndi anthu okwiya atagwidwa akuba zipangizo za khebo za lamya pamalo omwe ali pafupi ndi pamene afera pomwe paonetsa kuti anali atayamba kale kudula ma khebowa potengera kuti mmanja mwawo mukuonetsa atavala zozitetedzera (gloves) zomwe anavala munthawi yomwe amayamba kuchotsa zipangizozi.

18/09/2025

Atumbukafe pokhapo pochotsa soya pieces pa K80 kufika pa K900 zinawakwiyitsa πŸ˜…πŸƒ

Tchana ✊
18/09/2025

Tchana ✊

Sungabese bundle yimboyi  yanyatwa πŸ‘‡πŸ‘‡
13/09/2025

Sungabese bundle yimboyi yanyatwa πŸ‘‡πŸ‘‡

This song is composed & written by "OmmaDizzy" and it produced with "ClemDash OntheMix & Ace tee beat

OmmaDizzy
13/09/2025

OmmaDizzy

This song is composed & written by "OmmaDizzy" and it produced with "ClemDash OntheMix & Ace tee beat

Address

Matawale
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chinamwali Sounds posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share