Lai

Lai Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lai, Digital creator, Zomba.

Incase You Missed it 👨‍⚖️Peter Sambo vs BushiriMwaipatsa iti?
16/04/2026

Incase You Missed it 👨‍⚖️

Peter Sambo vs Bushiri

Mwaipatsa iti?

Sindizatopa kunena kuti zikomo Allah chifukwa iye satopa kundidzutsa ndi moyo
14/04/2026

Sindizatopa kunena kuti zikomo Allah chifukwa iye satopa kundidzutsa ndi moyo

Zizayenda official music video is out now
10/04/2026

Zizayenda official music video is out now

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

12/03/2026

I got over 500 reactions on one of my posts last week! Thanks everyone for your support! 🎉

02/03/2026

Ndinapangidwa hack komano ndapanga recover

kungomuthandiza mwa self container
27/02/2026

kungomuthandiza mwa self container

Theba yatinyamulatu thawi yayitali moti inatopa nafe
26/02/2026

Theba yatinyamulatu thawi yayitali moti inatopa nafe

26/02/2026

Good morning

Malawi ndi dziko limodzi mwa mayiko wosawuka muno mu  Africa 🌍 MOTi lilipa nambala 3 kumayiko ovutikisisa pa nambala 1 P...
25/02/2026

Malawi ndi dziko limodzi mwa mayiko wosawuka muno mu Africa 🌍 MOTi lilipa nambala 3 kumayiko ovutikisisa pa nambala 1 Pali Burundi kmaso pa nambala 2 Pali south Sudan komabe Malawi ndi dziko latendere kmaso anthu ake sakonda nkhondo I love Malawi mwina tizalemera Mulungu ND amene akuziwa. 🇲🇼

"DZUKANI KWACHA☀️🫵"MLANDU WA MWANA WA MALEMU WA PRESIDENT WAMKALE WA DZIK0 LA ZIMBABWE R0BERT MUGABE'S S0N YEMWE ANAMBER...
25/02/2026

"DZUKANI KWACHA☀️🫵"

MLANDU WA MWANA WA MALEMU WA PRESIDENT WAMKALE WA DZIK0 LA ZIMBABWE R0BERT MUGABE'S S0N YEMWE ANAMBERA GARDEN B0Y WAKE KU JUBECK

Mt0lankhani H0pewell Chin0,n0 anakapanga chipikisheni ( research) ndip0 adapeza kuti Chatunga Mugabe Hyde Park H0use , nyumba yake y0mwe akukhara Mwana wa Mugabe inagulidwa mu Chaka cha 2017.

Pamene bamb0 ake akaladali ndi Mphanvu ( when his father was still in p0wer) , Ndip0 Antigura kwa Ndalama z0kwana R43, Million pafupi-fupi US$3.2 Million Dollars, pa nthawi y0.

Ndip0 Chatunga ata0nekera ku C0urt , ndip0 anavala kasukumba k0dula manja ( a Moncular Maya puffer) y0mwe mteng0 wake US$2,556 pafupi-fupi Ndalama z0pitilira ( R40,000 Rand) ch0nvala chim0dzi .

Ndalama ya ch0nvala chim0dzi chimenechi ili ngati Malipir0 0nse amunthu 0gwira ntchit0 b0ma ( same like civil servants saraly yearly) chaka ch0nse dzik0 la Zimbabwe.

Ndiye apa mwaw0na n0kha andalewa z0mwe amapanga sindikutchula dzala munthu wa ndale aliyense wa ku Malawi, k0ma ndati andale.

Address

Zomba

Telephone

+265994648790

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lai posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share