MSCE Preparation

MSCE  Preparation 𝐅𝐚𝐢𝐥𝐢𝐧𝐠 𝐭𝐨 𝐩𝐫𝐞𝐩𝐚𝐫𝐞 𝐢𝐬 𝐬𝐚𝐦𝐞 𝐚𝐬 𝐩𝐫𝐞𝐩𝐚𝐫𝐢𝐧𝐠 𝐭𝐨 𝐟𝐚𝐢𝐥.
(2)

10/06/2026

View once akumatheka koma ku WhatsApp so let's go kumeneko...
Join final coaching,
0999136433

Kuloweza ichi muti zitheka?
10/06/2026

Kuloweza ichi muti zitheka?

10/06/2026

Anthu akagona mundiuze ,, pali zoti tikambirane Akuluakulu

Mayeso ana aja amaliza lero , mwasalatu Akuluakulu inu Zikomo
10/06/2026

Mayeso ana aja amaliza lero , mwasalatu Akuluakulu inu
Zikomo

10/06/2026

Pena ngati ndinene kuti mungochedwa , zenizeni simungazipeze mophweka

10/06/2026

Potumiza pic ya view once ndi pati?

10/06/2026

Amene mumakumana face to face discussions ndipo mumakhala kutali,
Mukakumana muzitihalla pa number iyi 0999136433
Call or WhatsApp call ,
Ndipo tizikhala tikukuthandizani mogwirizana ndi zimene gulu lanu likuchita pomalizira tizipereka ma tips angapo kwa week iyi,, zonsezi mzaulere,
Lero amene muli ready mundiyankhula ku WhatsApp

10/06/2026

Ifetu panopa tili chikwanekwane. ena munadandaula kuti sitimakuyankhani ma messages anu ku WhatsApp, taonjezera ma admin,
Ngati mukudziwa kuti muli Zomba, Blantyre, Thyolo,Mulanje, Phalombe Chiladzulo ,Mangochi ndi Machinga ndipo muli ndi gulu lomwe mumapanga ma discussions kumeneko, and mumatipanga follow pa page ino, tiuzeni tikupezeni kumeneko week before exams ,tidzacheze face to face ,macheza athu adzakhala masenga oopsa kwambiri okuthandizani kudzakhodza mayeso, Zambiri tikambirana 0999136433

Omwe simukwanitsa join our online classes lero mosapitirira mmawa,,

09/06/2026

Mulipo angati omwe mwakonzeka to pay fee ya nthawi yomwe yasalayi,,, chifukwatu malo akatha basitu ma updates muzidzangomvera pa Facebookpa ,,
Tabwerani ku inbox 0999136433 WhatsApp

09/06/2026

1. A village had a fish pond, two hectares of land which is degraded, millet and ground nuts,
and poultry farm. Explain five ways in which the farmer would use the resources to mitigate
climate change

2. Explain five effects of soil structure on crop production

3. Explain any five importance of agricultural development agencies

Address

Online School (+265999136433)
Zomba

Telephone

+265999136433

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MSCE Preparation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MSCE Preparation:

Share

Category