NMS TV

NMS TV 🎀 NMS TV
An Islamic media platform supporting New Muslims in Malawi
πŸ“Ί Da’wah β€’ Interviews β€’ Outreach
πŸ“ž +265 986 691 40

06/05/2026

πŸš€ β€œTiyeni Tikulitse NMS TV Limodzi – Follow, Like & Subscribe!
Elias M. Pemba Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Agogo Amuna Yunus James Becks Ibrahim Joyson Kev MISI Sherif Qassim Gamah Idris Habeeb

05/05/2026

The Truth About Hijab & Obedience to Allah – A Powerful Message to Muslim Women Yunus James Agogo Amuna Elias M. Pemba Joyson Kev Malawian Arabic Teacher Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Abdullah Moyo William Jazeel Sherif Qassim Gamah Abdul Rasheed Hassan Idris Habeeb Becks Ibrahim

04/05/2026

πŸ”₯ ZIFUKWA ZOMWE ENA AMACHINYOZA CHISILAMU πŸ”₯

πŸ‘‰ Kodi n’chifukwa chiyani anthu ena amalankhula zoipa pa Chisilamu?

πŸ‘‰ Ndi kusamvetsa kapena ndi zina zobisika?
πŸ‘‰ Yankho lilipo mu video iyi!
πŸ“’ @ Khalani tcheru… uthenga wamphamvu

πŸ“Œ Share ndi anzanu kuti onse aphunzire
chowonadi.https://www.facebook.com/share/1JKXzzJ4gE/ Yunus James Agogo Amuna Idris Habeeb Elias M. Pemba Malawian Arabic Teacher Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Joyson Kev Becks Ibrahim Sherif Qassim Gamah Abdullah Moyo William Jazeel Abdul Rasheed Hassan John Nmstv Sankhani

30/04/2026

πŸ”₯πŸ”₯ UTHENGA WAMPHAMVU KWA ASILAMU – KHALANI OLIMBA MTIMA! πŸ’ͺπŸ•Œ Idris Habeeb Elias M. Pemba Becks Ibrahim NMS TV

29/04/2026

UTHILA KUWILI ✍️✍️✍️ NMS TV

πŸŒ™ NEW MUSLIM STORY | INSPIRING JOURNEY πŸŒ™Meet Pondani Thamangisa, an 81-year-old from Phalombe, T/A Kaledzera, Village Ch...
26/04/2026

πŸŒ™ NEW MUSLIM STORY | INSPIRING JOURNEY πŸŒ™

Meet Pondani Thamangisa, an 81-year-old from Phalombe, T/A Kaledzera, Village Chikomola β€” a story that touches the heart and inspires the soul.

Pondani once belonged to the CCAP church, but in the later years of his life, he made a powerful and courageous decision: he embraced Islam. Despite his age, he did not hold back. Instead, he dedicated himself to learning β€” spending one full month studying the basics of Islam.

What makes his story truly remarkable is his determination. At 81, he learned how to perform Swalah and understands many important teachings of a Muslim. This shows that it is never too late to seek the truth and follow the right path.

Life has not been easy for him. He lives alone and provides everything for himself. After accepting Islam, some people mocked him, saying he is too old and that such changes are for the young. But Pondani did not give up. He remained strong, focused, and firm in his faith.
He is a man of great courage and resilience.

πŸ™ A HUMBLE APPEAL Pondani needs support. Since he lives alone, any assistance can make a big difference in his life β€” whether it is food, clothes, or other basic needs.

If you are able to help, please reach out:
πŸ“ž Call / WhatsApp: +265 986 691 403
πŸ‘€ Contact: John Sankhani

β€œGuidance can come at any time β€” what matters is the heart that accepts it. Idris Habeeb Agogo Amuna Yunus James Joyson Kev Elias M. Pemba MISI Becks Ibrahim Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Abou sufian khatweeb dawood Abdullah Moyo William Jazeel Abdul Rasheed Hassan Dawah Vision Che Mandota - Dr J.S.Chikakuda

24/04/2026

Moyo wanga wasintha kwathunthu! 😳 New Muslim Story

19/04/2026

Anthu Akusokonekera: Kusintha Malamulo a Mulungu ndi Maganizo Awo
Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Malawian Arabic Teacher Agogo Amuna Yunus James Sherif Qassim Gamah Abdullah Moyo William Jazeel Blessings Mponda

19/04/2026

May Allah make it easy for all of us..

✨ CHISILAMU NDI CHIYANI?Chisilamu ndi chipembedzo chowonadi chomwe chimaphunzitsa kupembedza Mulungu mmodzi yekha (Allah...
18/04/2026

✨ CHISILAMU NDI CHIYANI?

Chisilamu ndi chipembedzo chowonadi chomwe chimaphunzitsa kupembedza Mulungu mmodzi yekha (Allah) popanda kumphatikiza ndi china chilichonse.

🀲 Kodi munthu akabwerera ku Chisilamu amafunika chiyani?
Amafunika kulandira chikhulupiliro chenicheni (Shahada), kuphunzira za chipembedzo, ndi kuyamba moyo watsopano wotsatira malamulo a Allah.

πŸ“š Ndi udindo wathu kuwaphunzitsa
Tiyeni tigwire ntchito limodzi pothandiza ndi kuphunzitsa abale athu atsopano kuti akule mu chikhulupiliro.

🌍 Uthenga kwa omwe si Asilamu:
Tikukuyitanani ku chipulumutso β€” Chisilamu.
Dziwani choonadi, phunzirani, ndipo yendani pa njira yolungama.

πŸ“Ί FOLLOW NMS TV (New Muslim Story)

- YouTube
- Facebook
- TikTok

πŸ‘‰ Phunzirani zambiri, limbikitsani chikhulupiliro chanu, ndi kugawana uthenga wabwino.

🌍 NMS TV – New Muslim StoryAlhamdulillah, anthu ambiri akulowa Chisilamu kudzera mu Da’wah. Izi ndi kupambana kwakukulu ...
17/04/2026

🌍 NMS TV – New Muslim Story

Alhamdulillah, anthu ambiri akulowa Chisilamu kudzera mu Da’wah. Izi ndi kupambana kwakukulu komanso madalitso ochokera kwa Allah.
Koma pambuyo polowa Chisilamu, ma New Muslim ambiri amakumana ndi mavuto ambiri.

Amasowa maphunziro a Chisilamu, zovala zozilemekeza, komanso zinthu zofunika pa moyo. Ena amanyozedwa ndi kusiyidwa ndi anzawo ndi mabanja awo.

Ife a NMS TV, tili patsogolo pothandiza ndi kulimbikitsa ma New Muslim ambiri kuno ku Malawi. Timawatsogolera ndi kuwathandiza kuti akhale ndi moyo wabwino mu Chisilamu.

🀝 Khalani mbali ya ntchito yabwinoyi
πŸ“² Tsatirani page yathu kuti muzilandira nkhani zambiri zolimbikitsa
❀️ Tithandizeni NMS TV momwe mungathere
Follow β€’ Share β€’ Subscribe

16/04/2026

Nkhani Zoona za Ma New Muslim – Malawi πŸ‡²πŸ‡Ό & Mozambique πŸ‡²πŸ‡Ώβ€
Idris Habeeb Malawi Muslim motivate speech and Tidziwe chisilamu chikutinji Malawian Arabic Teacher Agogo Amuna Abdullah Moyo William Jazeel Sherif Qassim Gamah

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NMS TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category