MANJE CCAP TV

MANJE CCAP TV Informações para nos contactar, mapa e direções, formulário para nos contactar, horário de funcionamento, serviços, classificações, fotos, vídeos e anúncios de MANJE CCAP TV, Canal de TV, MANJE, Chiúta.

Aroma 5:7Sizichitika kawirikawiri kuti munthu wina afere munthu wolungama, ngakhale kuti chifukwa cha munthu wabwino win...
06/01/2026

Aroma 5:7
Sizichitika kawirikawiri kuti munthu wina afere munthu wolungama, ngakhale kuti chifukwa cha munthu wabwino wina atha kulimba mtima kumufera.

[Mika: 2:1 Tsoka kwa amene amakonzekera chiwembu, kwa amene amakonzekera kuchita zoyipa usiku pa mabedi awo! Kukacha mma...
25/12/2025

[Mika: 2:1
Tsoka kwa amene amakonzekera chiwembu, kwa amene amakonzekera kuchita zoyipa usiku pa mabedi awo! Kukacha mmawa amakachitadi chifukwa ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.]

Tisachimwe pa chisangalaro chathu,, ndife akristu.
mawu amati muzonse zimene tichita tilemekeze nazo mulungu.

Mwaswera bwanji okondedwa mwa ambuye wathu yesu Christo. Tiphudzile za ana awiri wosiyana makolo                   ANA Y...
07/12/2025

Mwaswera bwanji okondedwa mwa ambuye wathu yesu Christo.

Tiphudzile za ana awiri wosiyana makolo

ANA YA SATANA/MDIEREKEZI
Mau akunenelatu za mawonekedwe ndi zochita za Ana ya satana/amdierekezi.
Ndiwofanana ndi abambo awo , monga muwona yhn 8vs44 akuti iwo ndi wakupha, alibe choonadi, ndiwabodza .

Yohane 8:44
Inu ndinu ana a mdierekezi. Iye ndiye abambo anu ndipo mukufuna kuchita zimene abambo anuwo amakhumba. Iye anali wakupha kuyambira pachiyambi, sanasunge choonadi, pakuti mwa iye mulibe choonadi. Pamene Iye anena bodza, amayankhula chiyankhulo chobadwa nacho, popeza ndi wabodza ndipo ndi bambo wa mabodza.

ANA YA MULUNGU
Mau akunenelatu za mawonekedwe ndi zochita za Ana ya a mulungu
Ana a mulungu amanvera ndi kuchita mau ya mulungu.

Yohane 8:47
Munthu wochokera kwa Mulungu amamva zimene Mulungu amanena. Chifukwa chimene simumvera nʼchakuti, inuyo sindinu ochokera kwa Mulungu.”

KODI NDINU ANA ANDANI PAKATI PA MULUNGU NDI SATANA?___ yakhani kuma coment

Ana-ya-mulungu : samapha, ali ndi choonadi, sanama bodza ndipo amanvera ndi kuchita zimene mulungu akunena.wawo-ndi moyo osatha ku paradaise.

Ana-ya-satana. Amapha, alibe choonadi,amanama bodza,ndipo sanvera mulungu. Chawo-ndi-chiwonongeko/gahena.

Follow pa page yathu 🙏🙏🙏 ambuye wathu yesu Christo akudalitseni AMEN 🙏

11/11/2025

Endereço

MANJE
Chiúta
MANJE SEDE

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando MANJE CCAP TV publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar

Categoria