Chaxy beats

Chaxy beats Informações para nos contactar, mapa e direções, formulário para nos contactar, horário de funcionamento, serviços, classificações, fotos, vídeos e anúncios de Chaxy beats, Produtor/a musical, Mozambiqeu zambezia de milange, Milange.

05/03/2026

Kd mmaziwa kt kupanga
comment like share
Kumapangisa kt Facebook yanu
Izikula? Ena mukaona ma post azanu
Mmangodusa mukusalilatu

18/02/2026

abale muli ku tawoni ko thelele odyela mavutoyi sakoma kuno

16/02/2026

AKAZI ALI NGATI MPUNGA 🍝🥘 UTHA KUSANKHANA MODEKHA BWINOBWINO KOMA PAMAPETO PAKE UMATAFUNA MWALA

PILOT NDI BENGO‎‎Pilot Wina Ananyamula Amisala Okwana 200 Kuti Awapitise Ku America..Ndipo  Anthu Amene Anyamulidwa Mu N...
29/01/2026

PILOT NDI BENGO

‎Pilot Wina Ananyamula Amisala Okwana 200 Kuti Awapitise Ku America..Ndipo Anthu Amene Anyamulidwa Mu Ndegeyi Adali Kuti Misala yawo Nde Yafika Pakayakaya Ndipo M'modzi Mwa Amisala 200 wo Adali Bengo Ndipo Zidali Motele ...Ali Mundege Muja Amisala Adayamba Kupanga M'phokoso Lambili Zedi Kupatulapo Abengo...Ndipo Adaganiza Zopita Kusogolo Komwe Wakhala Pilot Uja ...Ndipo Zidali Motele

‎Abengo: Ase Ndufuna Ndiyendese Nawo Ndegeyi...

‎👨‍✈️Pilot; Ok ndizotheka Komano Choyamba Walese Kaye 'phokoso Anzako Ali kumbuyowo....

‎🧔 Abengo ; ouk Ndubwela Kae...

‎Patatha 18min Mu ndege Muja Munali Ziiii ....Kenako Bengo Anapitaso Kusogolo Kuja Ndipo Zidali Motele

‎Abengo; ase Ndipase Ndiyendese Fanz yonse Ndayikhazika Chete Uku!..

‎Pilot; Tadikila Kae Komano Wapanga motani Kuti Onse Akhale Cheteee???

‎Abengo; Ndinangosegula Kumbuyo ko Ndipo Onse Atuluka Panja ..I think Akulongololela Panjapo..

‎👨‍✈️ Pilot; 😲😲😲😲😲???.👇

https://www.facebook.com/profile.php?id=61586804182735

🦋MALOTO ABENGO ALI KUMWAMBA💔‎‎👼Angelo: Takulandirani kuno kumwamba ndipo simuzabweleraso paziko lapabsi!‎‎🧔Bengo: kusony...
25/01/2026

🦋MALOTO ABENGO ALI KUMWAMBA💔

‎👼Angelo: Takulandirani kuno kumwamba ndipo simuzabweleraso paziko lapabsi!

‎🧔Bengo: kusonyeza zoti apapa ndamwalira?

‎👼Angelo: Eya' ndipo mulindi machimo ambiri zimene zikusonyeza kuti inu mukupita kumoto bas!

‎🧔Bengo: Chonde Chonde ndikhululukireni ndibwelere padziko la pansi ndikalapeso machimo!

‎👼Angelo : ngati ukufuna kubwelera pa ziko lapansi ndekuti sukakhalaso munthu tikupanga kuti ukakhale nkhuku!

‎🧔Bengo: nde moti mpkana ndizikayikira madzira?

‎👼Angelo: eya uzikayikira mazirawo ' yesela uwone ngati ukukayika!

‎🧔Bengo: Etidi zikuthekadi😁!

‎ Angelo: ikiraso dzira lina!

‎🧔Bengo: zathekaso😁


‎Kenako Mosakhalisa anangova mbama theeeeeee kuchokela kwa Mkazi wake uku akukalipa avekele

‎👩Nkazi: Iwee Bengo zoona mene wakuliramu ungamanyele pogona?

‎🧔Bengo:😱😱💔

Osaiwala 👇

https://www.facebook.com/profile.php?id=61586804182735

Music producer

15/01/2026

Endereço

Mozambiqeu Zambezia De Milange
Milange

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Chaxy beats publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Atalhos

Compartilhar