10/08/2025
Koma azimayi kuma group uku muli nkunamizana eeesh ati yeast infection samapasilana komaso mankhwala ake ndi madzi ozizila okha 🤣🤣 tamapanganiko google panokha zinazi aaa mukatha mundipeze muzatenge chiswabu ndi cleanser anzanu akuchililatu kuno. 🤗