09/14/2026
Thomson Mpinganjira watsutsa malipoti oti watula pansi udindo wake ngati Mtsogoleri wa timu ya Mighty Wanderers kaamba koti timuyi sidachite bwino mu mpikisano wa CAF Champions League.
Times 360 Malawi yatsimikiza nkhaniyi.
Lamulungu, Wanderers yatuluka mu Champions League itagonja ndi Simba SC 7-1. 📸 Social Media