09/08/2026
Sukulu za Katolika, ndi zomwe zakhonzetsa bwino, pa mayeso a folomu 4 a chaka chino...
Malingani ndi bungwe Malawi National Examinations Board (MANEB), komanso unduna oowona zamaphunziro.
Zasonyeza kuti, ma sukulu a katolika ndiomwe anyambitsitsa yogheta makolo ochuluka chaka chino, pokhozetsa ana awo mochititsa chidwi. Kumasukuluwa kwatuluka chiweerengelo chochuluka cha ma distinction komanso chiwerengelo cha okhonza ochuluka.
in conjunction with the Ministry of Education, Science and Technology, has today released the 2026 MSCE examination results, with 111,510 of 188,169 candidates passing, representing a national pass rate of 59.26 percent.
The top ten schools are:
Top Ten ya sukulu zomwe zachita bwino.
1. St Mauritius, Rumphi — 65.00%
2. Ludzi Girls, Mchinji — 50.13%
3. St Kizito Seminary, Dedza — 49.71%
4. Likulezi Catholic Boys, Phalombe — 49.00%
5. Karonga St Mary’s Girls, Karonga — 48.65%
6. St John Bosco, Mzimba South — 47.08%
7. Likuni Boys, Lilongwe West — 45.10%
8. Marist (Pvt), Dedza — 43.79%
9. St Patrick’s Seminary, Rumphi — 42.74%
10. Chaminade, Karonga — 42.11%
Pa ana okwana 188, 169 omwe adalemba mayeso, ana 111, 510 ndi omwe akhoza kuimirila chiwerengelo chokwana 59.26 pa 100.
Ndipo masukulu omwe alepheretsa ana onse, ndanda wawo uli motere:
1. Magnus (Thyolo, 8.33%)
2. Ntonya(Blantyre Urban 12.50%)
3. Prema (Thyolo, 13.04%),
4. Nkhande (Machinga, 13.16%)
5. Ajemson (Lilongwe City 14.29%)