
27/08/2025
Dear Rashley Mw
Kupepesa sikupusa, ndiwe munthu m,bale I hope you know ukupepesa kwa anthu oti amapanga ndipo anapanga zinthu zoyipa kuposa iweyo.
But as a man you need to take accountability of your actions and apologize. Dont beat yourself up.
Ukupepesa kwa anthu oti tikuyenera kupepesa kwa anthu ena mnjira zambiri. Nobody is holy okupanga judge ndi mulungu koma ngati anthu ena angakupange judge ndekuti akuzimva kusachimwa pamaso pa mulungu. Good luck
Mikozi