Nkhwinimba Online

Nkhwinimba Online Arts and entertainment
(3)

02/09/2026

Usiku wanu ukuyenda bwanji ma guy?

Dress lowonetsa Dzuwa, Nyanja, ndi Mapiri. Apa Ireen Navicha wayipatsa moto ku Miss World.
02/09/2026

Dress lowonetsa Dzuwa, Nyanja, ndi Mapiri.
Apa Ireen Navicha wayipatsa moto ku Miss World.

Baby mama wa late Sidik Mia akuti mpaka lero sanalandile thandizo lililonse kuchokera kwa Mia family.
02/09/2026

Baby mama wa late Sidik Mia akuti mpaka lero sanalandile thandizo lililonse kuchokera kwa Mia family.

02/09/2026

Koma zowopsa šŸ˜…

Amalawi ambiri atutumuka ndimene ma Benz akugulidwira pa Malawi pano mwakathithi, anga bodya zosenzi chifukwa chakuti ch...
02/09/2026

Amalawi ambiri atutumuka ndimene ma Benz akugulidwira pa Malawi pano mwakathithi, anga bodya zosenzi chifukwa chakuti chuma cha dziko lino pansi pa ulamulilo wa Mkulukutamoyo chikukozeka ndipo chayamba kuyenda bwino!

Zimatero ndithu mu ulamulilo wa APM amalawi ambiri amatukuka kwambiri coz even poverty rate yatsikatu m'dziko muno.

Economy ili stable!
APM A Great Return of Proven Leadership

02/09/2026

šŸ¤•

Habbakkuk Ali mtika mwenimwenišŸ‘Nthawi imafika basi
02/09/2026

Habbakkuk Ali mtika mwenimwenišŸ‘
Nthawi imafika basi

DO NOT BRING POLITICS INTO YOUR WORK  MUKHITOMzuzu Police Ground | 2 September, 2026.Honourable Peter Mukhito, who is al...
02/09/2026

DO NOT BRING POLITICS INTO YOUR WORK MUKHITO

Mzuzu Police Ground | 2 September, 2026.

Honourable Peter Mukhito, who is also the Minister of Homeland Security and Secretary General of the Democratic Progressive Party (DPP), has urged officers working in the Police, Prison and Immigration departments not to bring politics into their work, saying this hinders the development of the country.

Speaking at Mzuzu Police Ground, Mukhito said politicians come and go, and therefore the officers should understand the nature of their work in order to ensure that the vision of the country's leader, Professor Arthur Peter Mutharika, is achieved.

Among other things, Mukhito urged all officers in the Police, Immigration and Prison departments to avoid acts of dishonesty and corruption, saying the law will take its course against anyone found engaging in such practices.

Mr Speaker sir
02/09/2026

Mr Speaker sir

02/09/2026

Prophet Habakkuk kulandila ulemu kuchokera kwa azimayi aku police.

Address

Johannesburg
46614

Telephone

+27724745081

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhwinimba Online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share