Doc 2030

Doc 2030 Welcome to Nkhoma university Vibes, Follow for more fun and memories

31/10/2025

Kumeneko akutuluka?
🙄

NCE TV , Nalikule College Of Education  Nkhoma University imamenya kwambiri 🔥😃, Osazapanganso chibwana 🤣 Uthenga watipez...
30/10/2025

NCE TV , Nalikule College Of Education Nkhoma University imamenya kwambiri 🔥😃, Osazapanganso chibwana 🤣
Uthenga watipeza!!!



It's Wednesday!!Introducing the stunning Miss Nkhoma University 🔥Our friends from Nalikule College Of Education     NCE ...
29/10/2025

It's Wednesday!!
Introducing the stunning Miss Nkhoma University 🔥

Our friends from Nalikule College Of Education NCE TV show us Miss Nalikule in the coment section
Tulutsani Wanuyo timowone!!


Apapatu our friends from Nalikule College Of Education  Ati anali ndi Social Weekend amabweza Dis/beef ija . 💔🤣💀.Kod uku...
26/10/2025

Apapatu our friends from Nalikule College Of Education Ati anali ndi Social Weekend amabweza Dis/beef ija . 💔🤣💀.

Kod ukuku ndi kwa Mbambande 🤣😃
Nde bolanso anakango ujenitu🙄

Nkhoma University imamenya kwambiri 🔥


24/10/2025

It's a Friday!!
Where are you !! 🍻

24/10/2025

This is how students at Nalikule College Of Education prepare for exams. 🤣💔

24/10/2025

Kodi Azathu aku LUANAR ada awawa Bunda Muluzi Tivi Diss/ Beef akupanga wokha Kapena LUANAR yonse yawatuma anthu ku inbox akufunsa 🙄.


We've just reached 2K followers! Thank you for continuing support. We could never have made it without each one of you. ...
23/10/2025

We've just reached 2K followers! Thank you for continuing support. We could never have made it without each one of you. 🙏🤗🎉


Munthu Sungamangosamba Madzi apa Tap , borehole Moyo wako wonse Time imakwana kukasambako Madzi ambiri.This Saturday inu...
22/10/2025

Munthu Sungamangosamba Madzi apa Tap , borehole Moyo wako wonse Time imakwana kukasambako Madzi ambiri.

This Saturday inu !!!
Tiyeni Tiyeni!!
3 days left

20/10/2025

Uyu Mukuti Muluzi Tivi Mulandeni phone 🤣💔

Anzathu a Ku MZUNI , MUBASI Mulipo pa mudzi pano ?

Ife chete kuma stand!!

18/10/2025

LUANAR vs Domasi Diss/Beef 💔💀

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Doc 2030 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share