
23/01/2025
APM truly deserves respect ✅
I can confidently say APM is the Most Educated and Democratic President Malawi has ever had.
Kaya wina avomeleza Kaya ai koma bwanawa munthawi Yao Kwacha ndi Dollar was around 700 , mafuta agalimoto around 600 per litre and panalibe zoti mafuta kulibe , Feteleza was around 25 thousand .
Kodi nkulakwa Kuyamikira kuti ntchito amatha? Olo utafuna kupanga debate koma pansi pa mtima ukuziwa ndithu kuti zimene ndanena nzenizeni.
Ngati wina sangayamike ndi ufulu wake koma na ine ndikuti ya Mnzako ikaima iyamikile.
Ine pachabwino I will always appreciate kwabasi. Pachoipa timanena ngati mitengoi ndaika ndikunama wina atsutse atchule ma figures.
You did your best sir. Kachamba says thanks for the service.