A F i S i

A F i S i Celebrity gossip & news

Jay Jay Cee Mw is Thebing in Theba
02/10/2024

Jay Jay Cee Mw is Thebing in Theba

1980 GangStaz
28/08/2024

1980 GangStaz

Big man wankulu in fresh 📸
27/08/2024

Big man wankulu in fresh 📸

😅 Ukagula Thiisheti usakuziwa zomwe yukamba 😆
23/08/2024

😅 Ukagula Thiisheti usakuziwa zomwe yukamba 😆

22/08/2024

JAY JAY CEE & MADY P OUT OF MABILINGANYA EMPIRE

Don Gogo Has Announced
👇👇

**Important Update To All Mabilinganya Empire fans**

Today marks a new chapter as Jay Jay Cee officially resigns from the Mabilinganya empire crew to pursue a solo career. After 11 incredible years with the crew, he expressed his heartfelt gratitude to me for welcoming him to Mabilinganya empire and introducing him to the artists. He also thanked the crew for everything they did for him during his time with them.

As for me, I have also decided to part ways with the Mabilinganya brand and will not be recording any songs under their brand and also I will not be attending any show under their brand because of some of my personal reasons. I just want to concentrate on pushing artists under Gogo Movement.

My the almighty God continue guiding them when they are still proceeding with the mission. THANKS

Babatunde Adepoju all the way ⚡⚽
21/08/2024

Babatunde Adepoju all the way ⚡⚽

Cheteee! ku slayer pa M1 😎.... Koma Joyisi 😒
21/08/2024

Cheteee! ku slayer pa M1 😎.... Koma Joyisi 😒

SAD : 😥 Chipepeso ndi chilimbitso kwa rapper Macelba Marley who has lost his father today. 💔
20/08/2024

SAD : 😥 Chipepeso ndi chilimbitso kwa rapper Macelba Marley who has lost his father today. 💔

Anthu awiri a Mulungu 😐
19/08/2024

Anthu awiri a Mulungu 😐

19/08/2024

" Olo ku Maliro a Mafunyeta ine sinakuoneko " Warge Dada Wanangwa Phiri wamung'alura Major Star
👇

Kuchokera tsiku lomwe King Shaka.... Mafunyeta anatisiya kwakhala kukukonzedwa show yomukumbukira chaka ndi chaka... chikonzelochi sichinangopangidwa ndi Mabilinganya Empiree Large payokha ayi... koma ananyamuka ndithu Chiso Dotolo Kachisomo... Gregory Comrade Tamnyata Mugala ndi ena angapo kukapempha chilolezo ku akubanja a Dancehall Legend Mafunyeta.. ndipo analolezedwa kutero.. kuchokera pamenepo mu commitee yachikonzeloyi mulinso mkulu wake weniweni (blood brother) wa Mafunyeta dzina lake Innocent Magalasi (Ras Inno) kusonyeza kuti chilichonse chomwe chikuchitika achibale ake a Maluli amakhala ali pompo... ku bank account yomwe anthu akufuna kwabwino amatithandizirako kuli signature ya Innocent Magalasi, mmodzi wamu Mabilinganya empire ndi Mtsikana wina ongokhalitsa naye mu area 18 muno... kusonyeza kuti kukakhala nganyase ku bankiku okatenga ndi anthu amenewawa...

Nde a Major Star munazalemba kuti akubanja kwa Mafunyeta amadana nayo show iyiyi ndipo ya chaka chinoyi ndiyomaliza... sibwino choncho man.. musokoneza anthu amene amaikonda ndi mtima onse show imeneyi..

Choti mudziwenso ndichoti anthu ena ali ku commitee imeneyiyi amaononga ndalama zao kuti chinthuchi ichichi chikatheke chonchija... nde kuyankhula mwayankhulako sikunandiwaze.. ngakhale Innocentiyo wakhumudwa nazo..

Inuyo munali ma friends ndi Maluli bhobho ndimakuonani komano bwenzi mukukondwera kuti Legacy ya Nyetha ikubalano zipatso...

Next year muzatigayire 3 million yoyambira kuti tizakwanitse kulipira malo aja timapangira show kupangitsa ma poster kulipira ma press briefing onse timachitawa kenakono muzizayankhula bwino.. chifukwa olo ku Maliro a Mafunyeta sindinakuoneniko

Zikomo

a Dad 🤝 Mayi Jane Ansah. Business as usual 😉
18/08/2024

a Dad 🤝 Mayi Jane Ansah.
Business as usual 😉

Titsitsi ta ELI Njuchi kungobhebhatu poti ndi celeb 😂Imagine ali mu street usakumuziwa. Achina Kell Kay sawaona iyeyu 🤔
18/08/2024

Titsitsi ta ELI Njuchi kungobhebhatu poti ndi celeb 😂
Imagine ali mu street usakumuziwa. Achina Kell Kay sawaona iyeyu 🤔

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A F i S i posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share