Malawi online

Malawi online Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi online, Blantyre.

Kwanukha linya kkkk
26/04/2026

Kwanukha linya kkkk

26/04/2026

Kunachema ku America

05/04/2026

Sindinaphe Grace Chinga Ndipo Sindinayankhulanepo Naye

__ Bushiri wati iye ndi Grace Chinga sanayankhulanepo kapena kukumana, koma wati panali anyamata ena ake atatu analemba Kalata ndikuigawa dziko lonse la Malawi ndikumanamizira kuti walemba ndi Miracle Chinga ndi M'chimwene wake Stevie yotchukitsa kuti Bushiri anapha Grace Chinga, iye wati za Grace Chinga samadziwapo kalikonse popezanso nthawi imeneyo anali ali ku South Africa.

Prophet Sheppard Bushiri watinso chakachino onse omutokosa mphuno ndi chikuni azingowamangitsa ndikuwatengera pakhothi,akakhala ena aja akungokhalira kukamba za iye aja akuti imene ija ndi misala ndipo akufunika ku mental akhala akumupemphelera kuti achile mwachangu.

22/03/2026

With Mikozi – I've just earned their Eni mudzi badge!

22/03/2026

Liema is a winner of Mzazi big brother

14/03/2026
01/03/2026

Tiloreni Nafe Tiyambe Kukhala Ndi Ma Nuclear komanso Ma Missile

__ President wa EFF ku South Africa Julius Malema wapempha mayiko aku ulaya kuti ayambe kuloleza mayiko aku Africa nawonso kukhala ndi ma nuclear komanso ma Missile popeza zinthu zikusintha nkhondo zapa ground zikutha,ndipo wapempha atsogoleri aku Africa kuti achangamuke.

Kuchokera m'chaka Cha 1996 Africa simaloledwa kupanga komanso kuyesa mabomba a nuclear ndipo palibe dziko lomwe lili ndi Bomba la nuclear ndipo ndimaiko 4 okha omwe amaloledwa kukhala ndi ma missile ongozitetezera chabe.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share