DPP News

DPP News Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DPP News, News & Media Website, .

21/04/2025

Pope Francis dies

Pope Francis of the Catholic Church has died today.

Vatican News has announced on their official social media pages.

According to Vatican News, Pope Francis has died aged 88 at his residence in the Vatican’s Casa Santa Marta.

Late Pope Francis real name was Jorge Mario Bergoglio.

He was from Argentina and was the first Latin American and first Jesuit to lead the Catholic

18/04/2025

Big shout out to my new rising fans! Charles Bandah

19/03/2025
Akufuna 5yrs ina k*t azangotimalizano tonse
25/02/2025

Akufuna 5yrs ina k*t azangotimalizano tonse

26/12/2024

𝗔𝗸𝘂𝗺𝗮𝗻𝗮 𝗻𝗮𝘇𝗼 𝘂𝗸𝘂

Atsogoleri a zipembezowa sanatchule mipingo yawo ndipo ati ndi kaamba koti iwo ndi anthu okhulupilira.

Ayankhula izi atafunsidwa mafunso ndi olemba nkhani omwe ali ku msonkhanowu.

Ichi ndi chidule cha momwe mafunso ndi mayankho zayendera;

Funso 1. Mwangozitchula mayina koma simunatiuze k*ti mwachokera mipongo iti?

: Musadandaule k*ti tachokera k*ti , mungodziwa k*ti ndife atsogoleri ampingo ndipo tabwela pamodzi ngati okhulupilira.

Funso 2. kodi zomwe mukuyankhulazi mwawafunsa akhristu anu kapena mukungozinenera ndipo mukusiyana pati ndi ojiya a chipani?

: Musatiwone ngati ojiya, inetu ndinapanga nawo mwambo wa send off ku mortuary maliro a clinician uja

Funso 3: Kodi mwayankhula nawo a Archbishop Msusa?

: Sitinayankhule nawo, iwo anayankhula pa gulu ndipo ifenso tawona k*ti tiyankhule pa kugulu

15/11/2024

Kuno kwathu mkovuta kwambiri...zimbudzi ma Border athu zolipila.mwachitsaso kumwanza ,ak*ti akafuna K300 k*t munthu akodze (azithandize)

    Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati pali kufunika kwakukulu k*ti dziko lino lichititse zokambirana k...
02/10/2024



Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati pali kufunika kwakukulu k*ti dziko lino lichititse zokambirana k*ti lipeze mayankho pa mavuto a ngongole zochuluka zomwe dziko lino liri nazo.

A Muluzi anena izi masanawu ku msonkhano waukulu wa chipani cha United Democratic Front (UDF).

A Muluzi ati ngongoleyi yomwe ndi yopyola K15 trillion, ndi chizindikiro choti chuma cha dziko lino sichikuyenda bwino.

Iwo ati pali kufunika kochita zokambirana ndikupeza mayankho chifukwa dziko lino posachedwa lifika pa ngongole zoopsa monga kumafika K19 trillion olo kufika K20 trillion kumene.

A Muluzi ati zikafika apa, pali chiopsyezo choti dziko la Malawi litha kudzayikidwa pa mndandanda wa maiko oshoteratu (bankrupt), ndipo ati izi ndi zoopsa.

30/08/2024

Ngati report tik*ti panalibe communication iliyonse ya ndege, Chakwera anadziwa bwanji k*ti ndege inauzidwa ibwerere ku Lilongwe? Anadziwa bwanji k*ti ili malo ak*tiak*ti poti communication pakati pa ndege ndi a Traffic control panalibepo? Anamuuza Chakwera k*ti ndege inabwezedwa itafika ku Mzuzu ndi ndani poti communication ndi ndege panalibepo according to report. Nchifukwa chani Chakwera analamula k*ti azipasidwa ma report a ndege yoti yakwera Tsogoleri wa chiwiri wa dziko every 4 hours? Amene amapereka ma report za ndege yoti inalibe communication ndi a pa ground.(Traffic control) ndi ndani? Mwachidule,,, akudziwapo kathu

30/08/2024

Namalomba waing'alula parliament momo Gotaniyo akumva 😂😂😂

31/07/2024

Ngakhale zitavuta bwanji, osaiwala mene anthu akuvutikila kmaso osaiwala k*t 2025,otiombola akubwela.
APM yemwe ndiyekhayo amakonda achinyamata, akubwela kuzatichosa mavutowa.
Malawi Chikangawa party yatizuza kwakwana

18/06/2024

Ma umboni ochuluka akuperekedwa APM 2025 bomaaaa!

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DPP News posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share