DAUD Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DAUD, Digital creator, 1strand Woodstock, Cape Town Southern Suburbs.

This kind of doctor is mad
24/01/2026

This kind of doctor is mad

how many did you see
24/01/2026

how many did you see

The driver of the scholar taxi that was involved in the horror crash in the Vaal that left 12 children dead on Monday, h...
24/01/2026

The driver of the scholar taxi that was involved in the horror crash in the Vaal that left 12 children dead on Monday, has been charged with culpable homicide and reckless and negligent driving.

USA DOOMS DAY PLANE YATULUKA Ndege mukuonai ndi ya USA. Yatuluka Lero.Ndegeyi anaipanga ndi malamulo Oti izingotuluka pa...
10/01/2026

USA DOOMS DAY PLANE YATULUKA

Ndege mukuonai ndi ya USA. Yatuluka Lero.

Ndegeyi anaipanga ndi malamulo Oti izingotuluka pakakhala nkhondo ya nuclear to protect USA Government.

The last time inaoneka kumaso kwa anthu was 51 Years ago. Sinayambe yaonekako kumaso kwa anthu . Lero yatuluka ndipo anthu aiona yayamba kuzungulila koma USA Government sinanene chilichonse .

Maiko ayamba kuchita mantha kuti something big chikuphukidwa pansipa

Dzina la ndegei ndi DOOMSDAY

Your fastest, latest and trusted war page
βœ…

09/01/2026
Pamene Achina Trump Anakana Kupita ku G20 ku South Africa, Anzake a Theba Ailemekeza ndi Zokonzekera za Nkhondo yapa Mad...
09/01/2026

Pamene Achina Trump Anakana Kupita ku G20 ku South Africa, Anzake a Theba Ailemekeza ndi Zokonzekera za Nkhondo yapa Madzi.

Ma sitima ankhondo aku China komanso Iran afika mnyanja yamchere mdziko la South Africa kumene akuembekeza kukhala ndi training yoteteza sitima zapamadzi. Nayo Rasha ikuenera kutsikira komweko kukachita nawo zokonzekelaziπŸ™†β€β™‚οΈ

China ndiyomwe itsogolera zokonzekerazi zomwe cholinga chake ndikuteteza ma sitima onyamula katundu apamadzi. Maiko onsewa alinawo mgulu la BRICS.

Zinthunzizi ndizenizeni zitsulo za nkhondo kukhamukila pa Theba!

Mwati tsiku lina a Malawi sizidzatikhudza izi!?🧐

let's get 10k followers πŸš€πŸ’₯πŸ‘
09/01/2026

let's get 10k followers πŸš€πŸ’₯πŸ‘

Ii koma boys πŸ˜†
09/01/2026

Ii koma boys πŸ˜†

Address

1strand Woodstock
Cape Town Southern Suburbs
7785

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DAUD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share