POSHA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from POSHA, Digital creator, strand, Cape Town.
(2)

๐Ÿ”” Verified Worldwide News & Real Stories
๐Ÿ“ฉ Anonymous Inbox Stories Welcome
๐Ÿ’ก Advice โ€ข Life Lessons โ€ข Awareness
๐Ÿ˜‚ Entertainment & Humor
๐ŸŒ Inform โ€ข Inspire โ€ข Entertain

LANDLADY OFFICIAL PAGE POSHANA

21/08/2026

Ndi mamuna wosatha kuphikayo tizakuwona ukazakhala ndi mimba๐Ÿคฃ๐Ÿ’”

21/08/2026

Kwama Ex nonsee!!!

Pena mumagwidwa ndima close friends athu nkumaona ngati you will hurt us
Koma lero on behalf of my fellow boys ndati ndikuuzeni kuti anyamatafe tili ndi habit yoti mkazi tikamusiya or tikathana naye timavungirana ma cross
Ndizija mumadyedwa ndi crew yonse Inu nkumaona ngati zitipweteka ayitu
Even nambala yanuyo timawapasaso ndiife tomwe,ndikuwauzaso mmene akulowereni kuti zisavute kukunyengani
Nde ngati mumati mumafuna kuti zitiwawe mung'omboka chabe
Mutenga nazo zosatenga๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜ซ๐Ÿ˜‚๐Ÿ’”

21/08/2026

Girls inayake be like, 'you deserve better sis' telling her fellow HULE. Kuchiona chi sisicho chinataya mimba 6, mauka phwii, chagonedwa ndi azibambo nkhani yake ya pizza, Malawi gin, bere linagwa kalekale chimimba chinafufuma ndi zimafuta za condom plus ma contraceptives pills mkati. komanso sis yoh olo zaka 25 sizinakwane aaa!! Muzikhala serious guys! apo ati chikusiya a young healthy, full portential guy matenda alibe komanso respectful with good upbringing ati ayi!!!! Akumuchedwesa, Sisi maliseche amatha awo muziganizire.๐Ÿ’€๐Ÿ’”๐Ÿ™Œ

Munthu amakulangizani bwinobwino mukatupitsaso mimba๐Ÿค”๐Ÿค” Umu  ndimene akuwonekera pano  esinati ๐Ÿคฐ
15/08/2026

Munthu amakulangizani bwinobwino mukatupitsaso mimba๐Ÿค”๐Ÿค”

Umu ndimene akuwonekera pano esinati ๐Ÿคฐ

๐Ÿ™Œ
14/08/2026

๐Ÿ™Œ

Eee km iPhone 12 amajambula bwino
14/08/2026

Eee km iPhone 12 amajambula bwino

Nkhuku ikudura ichi ndipasen 3pin ndili bangwe ๐Ÿฆ‰
14/08/2026

Nkhuku ikudura ichi ndipasen 3pin ndili bangwe ๐Ÿฆ‰

14/08/2026

Osamanditengeratu ine ndili pabanja komaso ndili ndiana๐Ÿฅฑ๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ

Dorothy naye wabweza chipongwe kwa temwah eishhh iyii sizitha mpk kale maganizo anu ndotan
14/08/2026

Dorothy naye wabweza chipongwe kwa temwah eishhh iyii sizitha mpk kale

maganizo anu ndotan

Kwacha timve nkhani zosiyana siyana iii
14/08/2026

Kwacha timve nkhani zosiyana siyana iii

Address

Strand
Cape Town

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when POSHA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to POSHA:

Shortcuts

Share