
26/09/2025
Nyamata mukumuona apayu waomberedwa ndipo wamwalira, izi zachitika ku Cape Town South Africa dera lotchedwa Gugulethu Barcelona lero pa 26 September 2025. Akuti nyamatayu amangodziyendera munthu wina anangotulutsa mfuti nkumuombera ndikuthawa koma atadziwitsa apolice anabwera ndipo atapanga chipikisheni achipexa chigawenga chomwe chachita izi ndipo amanga ali ku police. Mzimu wake uuse mu mtendere
Please note; uyu si mmalawi ndi nzika ya Ku Joni . tiyeni tikhale osamala kwambiri kuno ku dziko laweni tizitsogoza Mulungu patsogolo chifukwa ngati akuphana okhaokha kulibwanji ife oti amatida kale ππ€