04/09/2025
Kusinthasintha boma kumapangitsa kuti dziko lisatukuke, ndipo ife monga azitumiki a Mulungu tikunena kuti boma la Chakwela lipitilila chifukwanso latisamalila ife azitumiki potipatsa ngongole zochuluka kwambili zomwe maboma ena sanatichitile.