Ble knoertze

Ble knoertze Official page of ble knoertze

31/01/2026

゚viralシviralシfypシ゚viralシalシ

Pakadali pano ku Mthuzi anthu akulambira pamene oyimba osiyanasiyana akuyimba tsopano nyimbo za malambiro pane akudikira...
27/12/2025

Pakadali pano ku Mthuzi anthu akulambira pamene oyimba osiyanasiyana akuyimba tsopano nyimbo za malambiro pane akudikira matupi a Jue ndi Mac.

MAY THEIR SOULS REST IN PEACE 🕊️

27/12/2025

BLACK TEACHER ON TERRIBLE ACCIDENT

Shehe wamkulu, komanso odziwika bwino ku chipembedzo cha chisilamu, m'dziko la Nigeria,  Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wap...
27/12/2025

Shehe wamkulu, komanso odziwika bwino ku chipembedzo cha chisilamu, m'dziko la Nigeria, Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wapempha Dzikolo, kuti lithetse mgwilizano wake wa pakati pa Asilikali a Dzikolo ndi Asilikali a Dziko la America.

Shehe Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wapitiliza kufotokoza kuti kupezeka kwa Asilikali a Dziko la America, pa nthaka ya Dziko la Nigeria, ndi chiopsyezo ku Dzikolo.

Shehe Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wati ngakhale chili chinthu chofunika kwambiri kuthana ndi zigawenga, malinga ndi malamulo a chipembedzo cha chisilamu, ntchito yothana ndi zigawenga, ikuyenera ikuchitika ndi Anthu olungama, osati Anthu omwe ali ndi magazi m'manja mwawo.

Shehe Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wati zomwe lachita Dzikolo, ndi zinthu zolakwika kwambiri, kamba koti zigawenga sizimagwebana zinzake, kamba koti cholinga chake ndi kufuna kupeza zinthu zina.

Shehe Ahmad Abubakar Manhud Gumi, wati zomwe achita Asilikali a Dziko la America, ndi zinthu zomwe zibweletse magulu ena Anthu okhala ndi zida za nkhondo, ku Dziko la Nigeria.

(Olemba Grant Elisha Ngozo) 26/12/25

FUNERAL PROGRAM 🕊️💔
27/12/2025

FUNERAL PROGRAM 🕊️💔

MAY THEIR SOUL REST IN PEACE 🕊️
26/12/2025

MAY THEIR SOUL REST IN PEACE 🕊️

Breaking News Shehe oziwika bwino wa dziko la Nigeria Sheik Gumi wazuzula zomwe lapanga dziko la America ku Nigeria  🇳🇬....
26/12/2025

Breaking News

Shehe oziwika bwino wa dziko la Nigeria
Sheik Gumi wazuzula zomwe lapanga dziko la America ku Nigeria 🇳🇬...
iwo awuzilatu boma la Nigeria kuti liwauze ma America 🇺🇸 kuti asiyiletu zawozo apo bii azanong'oneza bondo...

Sheik Gumi akukhulupilila mukukambilana ndipo akuti zomwe lapanga dziko la America 🇺🇸 pophulitsa likulu la zigawenga zija ndikungokolezela kuti Zigawenga zambili zibwele ndipo Nigeria 🇳🇬 likhala bwalo nkhondo...

DADDY Donald Trump message yake iyi after perfect strike
26/12/2025

DADDY Donald Trump message yake iyi after perfect strike

USA Donald Trump Aphulitsa Nigeria uku. Iwo Aphulitsa head quarters ya gulu la zifwamba likupha akhilisitu zayambika ndi...
26/12/2025

USA Donald Trump Aphulitsa Nigeria uku. Iwo Aphulitsa head quarters ya gulu la zifwamba likupha akhilisitu zayambika ndithu

Merry Christmas family and friends 🎁🎄
25/12/2025

Merry Christmas family and friends 🎁🎄

22/12/2025

Akuti 1.9 Billion ipite bola Mcp inachoka boma

Address

Cape Town

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ble knoertze posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share