Jay Leez TV

Jay Leez TV With Jay Leez TV you Never Disappoint

Follow to day to get more info

05/03/2026

Ngati AI
゚viralシalシ

04/02/2026

Walandidwa nkazi

Obscene Facebook elders say they want to be President of MalawiLike seriously?
04/02/2026

Obscene Facebook elders say they want to be President of Malawi

Like seriously?

  😔A Edward Yotamu ali mu ululu owopsya kaamba ka chotupa chomwe anatuluka pa khosi m'chaka cha 2009.Iwo apempha anthu a...
29/01/2026

😔

A Edward Yotamu ali mu ululu owopsya kaamba ka chotupa chomwe anatuluka pa khosi m'chaka cha 2009.

Iwo apempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize munjira zosiyanasiyana.

A Vavada Mhango omwe akhala akuwathandiza bambowa, akhala akupita nawo ku chipatala cha Dedza ndi zipatala zina zolipilira kuchokera chaka chatha.

Iwo ati pakadali pano bambowa awagoneka pa chipatala cha Kamuzu Central ku Lilongwe komwe madokotala akuyembekezera kuwachotsa chotupachi.

mtsogoleri wa gulu lina la chifundo la nzika zokhala mu mzinda wa Lilongwe a Steven Masaiti apempha anthu akufuna kwabwino kuti awayikize bambowa m'mapemphero komanso kuwafikira ndi thandizo.

A Edward Yotamu ali ndi zaka 45 ndipo amachokera m'mudzi wa Kapesi, Mfumu yayikulu Kachere m'boma la Dedza.

Ofuna kuwafikila atha kuwapeza pa manambala awa: 0888626757/0994418114

Follow Jay Leez TV

29/01/2026

This is very Dangerous film how do you act My Chinese friend?

29/01/2026

Chinese Movies is sweet

NKHONDONkhondo imayamba pazithu zitatu bas1   = Mitundu imathandiza kuyambisa nkhondo kamba aliyese amakhala ndi zikhali...
28/01/2026

NKHONDO

Nkhondo imayamba pazithu zitatu bas

1 = Mitundu imathandiza kuyambisa nkhondo kamba aliyese amakhala ndi zikhalidwe zake Mmonga ngati izi
= Pakati Kuli Nyau
= kumpoto kuli zawo
= ku m'mwera kuliso zawo

2 = Zipembezo zili ndi kuthekera koti zingathe kuyambusa nkhondo Chifukwa mpingo uli onse uli ndi zomwe umasata monga
= Muslim Quran imakamba zawo
= Christian Bible limakamba zina

3 = Ngati anthu ena ali ochita bwino ena osalira pa chuma zili ndi kuthekera kwakukulu koyambisa nkhondo Chifukwa onsewa samaonerana kukonda wina ndi nzake pa zithu izii
= Ochitabwino amaona osauka ngati agalu
= osauka amaona anthu Ochitabwino ngati
ozikonda okha

MPHUZIRO ___ TIYENI TIZIKONDANA WINA NDI NZAKE CHIFUKWA ANATIBISIRA MAWA NDIPO ALIYESE NDI OFUNIKA KWA NZAKE IWE OCHITABWINO GALIMOTO YAKO IKAZATITIMIRA UZAFUNA ANTHU OSAUKA AKUTHANDIZE KUKAKHA MATOPE CHIMOZIMOZI OSAUKA IWE Sikulina ukazadwala uzafuna wa galimoto kuti akunyamulire kuchipatala

Pomaliza tonse sitingakhale Ochitabwino ndipo tonse sitingakhale Osauka zikomo

Address

22 Weimar Street Parow
Cape Town
7500

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jay Leez TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category