Okoma Atani Malunga TV

Okoma Atani Malunga TV welcome to Okoma Atani Malunga TV khalani omasuka kuyankhula zakukhosi kwanu comment, kuseka , kusangalala tose pamozi ngati one family.

My people my football ineso ndinali komweko bwanji simukamba zaine kuti Malawi women ikuwina muthawi yanga 🤣🤣🤣🤣🤣
12/08/2026

My people my football ineso ndinali komweko bwanji simukamba zaine kuti Malawi women ikuwina muthawi yanga 🤣🤣🤣🤣🤣

Naye Chimwemwe Mwenyemasi kaswiri opanga tsapato kokudaidaku walemba chocho akuti akumuza Phakela UMthakathi kuti apange...
12/08/2026

Naye Chimwemwe Mwenyemasi kaswiri opanga tsapato kokudaidaku walemba chocho akuti akumuza Phakela UMthakathi kuti apange organizer apite akaphudzise ma south african kupanga tsapato as a part of job creation kkkkkkk😂😂🤣🤣

Akuti job creation sitipangila pasewu kuthamanga opanda mayala kkkkkk zilikotu

Zathekatu basi Malawi kuzawina pamenepaja waku final basi .mwativesa kukoma atsikana.
12/08/2026

Zathekatu basi Malawi kuzawina pamenepaja waku final basi .mwativesa kukoma atsikana.

Koma lero kwachema eeeeeee South Africa yalembela kalata maiko angapo monga Nigeria ,Malawi ndi maiko ena kuti awabwedze...
12/08/2026

Koma lero kwachema eeeeeee South Africa yalembela kalata maiko angapo monga Nigeria ,Malawi ndi maiko ena kuti awabwedzele ndalama zawo zomwe awathandiza kutumiza anthu awo maiko mwawo ndipo ndalamazi akuzifuna as soon as possible.

Zovuta izitu achitila dala kuti maikowa Ave kuwawa ndipo ayambe kulimbikila kuwapasa achinyamata awo zochita komaso kuti apewe kulekelela anthu awo kupita maiko ena mutu mutu opanda passport or ma documents okhalila maikowa.

Kodi South Africa yapanga bwino?

Ma south african akulila kwambili amaona ngati akupanga create ntchito samaziwa kuti akuthesa ntchito.  Anthu ochuluka a...
12/08/2026

Ma south african akulila kwambili amaona ngati akupanga create ntchito samaziwa kuti akuthesa ntchito. Anthu ochuluka akuluza ntchito every day kuno ku south africa chifukwa ambili amapangidwa cover ndi ma Foreigners pamene folena akulimbikila or nzulu asamalimbikile amalandilabe ndalama basi koma pano mbola akufunika alimbikile yekha zomwe zikukanika chosatila akuchosedwa ntchito.

Akuyesa kuima misewu kusaka ntchito sizikutheka aliyese akungokweza glass basi

Pano kusowa kwa ntchito kunali pa 32.7% pano zafika pa 33.6% after 30 June abahambe Marching.

Tiwafunila zabwino zose.

Jasta ativuta osanama kuli meeting ya Sadc yomwe ikachitikile ku Durban pa 16 ndi 17 August Iye wakoza mademo akuti akaw...
11/08/2026

Jasta ativuta osanama kuli meeting ya Sadc yomwe ikachitikile ku Durban pa 16 ndi 17 August

Iye wakoza mademo akuti akawauze ma president amu Sadc yekha kuti sitikufunani chilungamo chimenechi abale?🙄🙄🤦‍♂️

11/08/2026

Malawi akhalabwanji Malawi opanda support ya dzika ya Malawi? Malawi siosauka dziko losauka silingakwanise kutenga nawo gawo pamipikisano yomwe imachitika pa dziko lapasi. Support Malawi

Machinga,Mangochi ndi Balaka week simunaiyambe bwino eshiiiii!!!Mayi watenga ndalamayo Mangochi tun off Sun hotel wabela...
11/08/2026

Machinga,Mangochi ndi Balaka week simunaiyambe bwino eshiiiii!!!

Mayi watenga ndalamayo Mangochi tun off Sun hotel wabela zungu wina ndalama yemwe amamukolopela mu room yomwe amagona ndalamayo anakasunga kwawo above 2 million apolice azipeza ndalamazo kumumanga.

Wanyamula ka toyi ka mfuti ndi Balaka wabela wakabaza njinga atamuza ukandisiye mudzi wakuti madzulo asanafike ulendo kumutulusila toy ngati futi kuzamufaka peper spiy matso kumubela koma apolice amugwila njinga yapulumusidwa apa akudikila amupase dzaka zokadya nyemba zaulele kumaula.


Zimayi wavala cha white ndi Machinga Liwonde hospital amumanga ponamizila ngati dokotala kumathandiza anthu pa chipatalachi zili zaboza atamufusa akuti amaphudzila. Apolice amutola kuti akamufuse mission yake ndiyotani

Kuli zinthuzi acheeeee!!!!!

Chipatala cha machinga Liwonde pamachuluka zochitika but why?Tsikana mukuonayi dzina lake ndi Tiyamike Mkandawile iyeyu ...
11/08/2026

Chipatala cha machinga Liwonde pamachuluka zochitika but why?

Tsikana mukuonayi dzina lake ndi Tiyamike Mkandawile iyeyu amasamba mamawa uliwose kumapita kuchipatalachi kumanamiza wanthu iyeyu ndi namwino . Tiyamike ali ndi dzaka 21 zakubadwa iye amalowa ma room apachipatalapa kumathandiza wanthu koma la 40 litakwana anthu anamukaikila ndipo anamupanikiza mafuso omwe analephela kuyankha zosatila zake iye anati akuzaphudzila za udokotala pa malowa.

Anthu anakatsina nkhutu apolice ya Liwonde omwe akwanisa kumanga tsikanayi kuti akamufuse mission yake inali yotani.

Not izi zimachitika pa dziko lose lapasi with different mission uyu sitiziwa mission yake.

11/08/2026

Why munthu ontchuka kungomwalila timati waphedwa? Kodi ukantchuka ndiye kuti usazafe?

Zimangovuta kuti timaganiza molakwika kuti mwina amayenela kufa ndi osauka basi komatu life sichocho tinabadwa ndipo tikudikila kufa basi kaya uli position yotani komabe tsiku la ifa yako likuza kozelatu kuti osala azalile mwachiyembekezo.

Kunja kuno ana achichepele akumwalila daily ena makolo anatisiya abale anthu ,ma brothers and sisters anasikila kulichete sikuti iwo anafuna ayi ka mulungu anakoza kuti zizakhala chocho.

Kulakwa kuti aliyese akafa kumati waphedwa pamene palibe umboni umbuli komaso zimayambisa nkhondo dziko anthu akufa everyday pa dziko lose lapasi ngati munthu waphedwa umboni ulipo okuphayo alandile chilango koma munthu ngati wamwalila ndi Mutu siyani mene zilili osawonjedzela ayi ambuye akudaliseni aliuese azafa anafa aja sanafune ayi.

Address

KZN South Africa And Malawi Chiladzulu
Durban

Telephone

+27843598650

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Okoma Atani Malunga TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Okoma Atani Malunga TV:

Shortcuts

Share