KODI Baibulo Limaphunzitsa Chiyan

KODI Baibulo Limaphunzitsa Chiyan pangani follow kuti tiziyendera limodzi. zikomo �

21/09/2025

AROMA 12:10

M'chikondano cha anzanu wina ndi mnzake mukondane ndi chikondi chenicheni; mutsogolerane ndi kuchitira wina mnzake ulemu.

Mwadzuka bwanji KODI Baibulo Limaphunzitsa Chiyan

20/09/2025

1 mbiri 16:24
Fotokozerani ulemelero wake mwa amitundu, zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.

Tisadane chifukwa cha kusiyana zochita aliyense munthu Ali ndi zokonda Monga ndale, mpira komanso kusiyana mpingo kumene kusatipangise kudana pakati pathu.

Tonsefe ndife ana amulungu 🙏

Mwadzuka bwanji KODI Baibulo Limaphunzitsa Chiyan fan's

You will win your battles in praise 🙏🏻
19/09/2025

You will win your battles in praise 🙏🏻

19/09/2025

Masalimo 139:10

Kungakhale komweko dzanja lanu lidzandisogolera,nilidzandigwira dzanja lanu lamanja.

Mwadzuka bwanji

18/09/2025

Verse of the day
John 3:16

For God so loved the world that he gave his one and only son, that whoever believes in him shall not perish but have eternal life.

Good morning 🌅

17/09/2025

Pamene tili busy kusatira mavoti tisayiwale kuika mulungu pasogolo kuti pakati pathu pakhale mtendere 🙏

04/08/2025

Good morning 🌄

Isaiah 60:22
When the time is right I, the Lord, will make it happen.

04/08/2025

Mwadzuka bwanji

MATAYU 4:4
koma iye anayankha nati, kwalembedwa, munthu sadzakhala ndi Moyo ndi mkate wokha, koma ndi mau onse akutuluka m'kamwa mwa mulungu.

Have nice day 🙏🙏

03/08/2025

Verse of the day

Akolose 3:2

Lingalirani zakumwamba osati za padziko ai 🙏

02/08/2025

Ambuye sazengereza nalo lonjezano, monga ena achiyesa chizengerezo; komatu aleza mtima kwa inu, wosafuna kuti ena aonongeke, koma kuti onse afike kukulapa.
((2 PETRO 3:9))

Address

Durban North

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KODI Baibulo Limaphunzitsa Chiyan posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share