1islam

1islam 1islam1ummah it's an Islamic TV channel that entertain, educate, inspire and promote islamic arts
(1)

31/05/2026

*
* part 1 of 10
* mutu... Tisakhulupilire *Zithumwa*
*
ndi


🔊➕🎦
#@ FB, TIKTOK, YOUTUBE*

Tiyeni tiyike ku status komanso kupanga share ma group uthengawu ndiofunika.

27/05/2026

? IMBANI +265 995992280

27/05/2026

EID ADHU LIVE FROM MANGOCHI KHUTBAH KOMANSO ULALIKI UPELEKEDWA NDI SH TAUFI DYTON KAZEMBE

 Pomwe ena akuswali mawali ndipo ena lachinayi tiyeni tisunge bata ndi mtendele osanyozana kapena kupasana maina achipon...
26/05/2026


Pomwe ena akuswali mawali ndipo ena lachinayi tiyeni tisunge bata ndi mtendele osanyozana kapena kupasana maina achipongwe tonse ndasilamu..

*Amawa tili nanu komanso a lachinayi tilinanu in sha Allah*

21/05/2026

*LECTURER SH. QASSIM WASIYA*
kuyankhapo zomwe ena akhala akufalitsa kuti mtumiki (S. A. W) sanasale kudya mu mwezi wa * Drulhijjah..

*💫1islamTV kusasiya aliyense m'mbuyo pa chilungamo*

19/05/2026

kufotokoza ubwino wa 10 days ya pa 💫1islamTV.
* Prod/Dir Sir
* Cam Hecium
* Sound. A. Matola
* Light V. Mazinga.

For more contact +265884294188

15/05/2026

KUCHOKELA KWA

10/05/2026

, Ma sheikh akulu akulu asonkhana ku Malindi_TURN_OFF_KU_MANGOCHI, Ndicholinga chowakumbusa asilamu zina mwa zithu zofunika zomwe muthu amatha kuiwala mosavuta

  likupatsilani  live and direct from  Ma Sheikh omwe mwakhala mukuwasowa aja lero ndi awa 👇👇    khalani nafe ndipo asat...
09/05/2026

likupatsilani

live and direct from


Ma Sheikh omwe mwakhala mukuwasowa aja lero ndi awa 👇👇





khalani nafe ndipo asatileni mwachidwi..

Uthengawu wapangidwa ndi sponsor ya padela dela choncho gawani uthengawu,
za Allah sitichitila umbombo.
Allah akudalitseni 👏

Address

Durban

Telephone

+27648123111

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when 1islam posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to 1islam:

Share

Category