Amir.tv

Amir.tv Amirddin Boko Mvula is Malawian digital journalist, trading under Amir.tv brand. We create an engaging content and make it trend. Simply "We make it trend"

www.youtube.com/

My approach is informal and engaging. Enjoy celebrity||Trending News

11/06/2026

Tipitanso😒

Ernest Mtawali asankhidwa kukhara mphunzitsi wa team ya Creck sporting club, pambuyo pochotsa a Eliya Kananji.
11/06/2026

Ernest Mtawali asankhidwa kukhara mphunzitsi wa team ya Creck sporting club, pambuyo pochotsa a Eliya Kananji.

Creck sporting club yachotsa ntchito mphunzitsi Eliya Kananji.Iwo sidaume wokha, apitanso wachiwiri wawo Saidi, komanso ...
10/06/2026

Creck sporting club yachotsa ntchito mphunzitsi Eliya Kananji.

Iwo sidaume wokha, apitanso wachiwiri wawo Saidi, komanso fitness trainer ndi Data analyst.

Kameza KuHes students object to the administration's last-minute decision to relocate to MUBAS from Kameza campus.
10/06/2026

Kameza KuHes students object to the administration's last-minute decision to relocate to MUBAS from Kameza campus.

Mwini wake wa Maranatha Academy Enerst Karonga, walonjeza kuthandiza mtsika waku mangochi, yemwe alipo yekha wamkazi yem...
10/06/2026

Mwini wake wa Maranatha Academy Enerst Karonga, walonjeza kuthandiza mtsika waku mangochi, yemwe alipo yekha wamkazi yemwe a kulemba mayeso pa sukulu yawo.

Akakhoza akaphunzira ku Maranatha ndipo azikalandira MK 500,000 pa teremu ngati upkeep, mpaka adzamalize school.

Hello followers!Tiyamba kufotokoza zokhuza ndale ndi chitukuko, [Politics and development]. Pomwe akadauro azifotokoza z...
08/06/2026

Hello followers!

Tiyamba kufotokoza zokhuza ndale ndi chitukuko, [Politics and development].
Pomwe akadauro azifotokoza za governance, politics and development.

Tizipanganso post zomwe nyumba dzikuluzikuru [mainstream media] zajambura ndiku lemba.

Tili mu dziko lomwe timalamulidwa ndandale, tiye tiyambe kuzitsata, ndale.

Zikomo!

Williams Gondwa walowera ku Jojo Fm. Wailesi iyiyi kupita mikhura ng'ona yokha yokha.JoJo fm, ndi wailesi yatsopano yomw...
08/06/2026

Williams Gondwa walowera ku Jojo Fm. Wailesi iyiyi kupita mikhura ng'ona yokha yokha.

JoJo fm, ndi wailesi yatsopano yomwe akuiyeselera, mwini wake ndi OG Issah, ili ku Maone, Blantyre.

Khuda writes"Malo anga ku flames aliko ndikwela ndege pompano  ndiyamba kusewela 🥶 tiyen tingositha coach ku afcon tipit...
02/06/2026

Khuda writes

"Malo anga ku flames aliko ndikwela ndege pompano ndiyamba kusewela 🥶 tiyen tingositha coach ku afcon tipitaso ambiri akugona mwina 🤣"

22/05/2026

Zambian tv presenter/Journalist, pakalapakala with English 😂 live on air📺

Anthu aku Blantyre, zaulere izi. Let's go!!!
22/05/2026

Anthu aku Blantyre, zaulere izi. Let's go!!!

Address

Beacon Bay
Blantyre
5241

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Amir.tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Amir.tv:

Share