Issac super love story

Issac super love story KUCHIMAKE KWA NKHANI ZOTHYAKUKA NDI ZOPHUNZITSA πŸ™πŸ™

*People who died yesterday had plans for today, so thank God for keeping you alive.*πŸ’”
16/08/2025

*People who died yesterday had plans for today, so thank God for keeping you alive.*πŸ’”

Mzimayi wina adamangidwa pa mulandu wakupha mamuna wake atasowa, adayesetsa kufufuza thupi la mamunayu koma silidapezeke...
06/08/2025

Mzimayi wina adamangidwa pa mulandu wakupha mamuna wake atasowa, adayesetsa kufufuza thupi la mamunayu koma silidapezeke.

Pakupita kwa zaka mzimayi uja adatuluka ku prison, kenako anthu ena adamuuza kuti amuona mamuna wake ku town ina ndipo akukhala ndi mkazi wina aliso ndi ana kumeneko.

Mzimayi uja adapita ku town yi ndi mfuti ndipo adamupeza mamuna wake uja ndipo adamuombela ndi mfuti kokwana ka 6 ndipo mamuna wake uja adafelatu pompo za serious tsopano.

Patabwela apolisi adamumangaso mzimayi uja, iye adawafusa apolisi kuti akumumangilanji, apolisi adamuuza kuti akumumangaso pa mulandu wakupha, iye adawafusa kuti mesa munthuyu ndidamupha kale ndipo ndidagwila kale ukaidi?

Inuyo muli judge nkhaniyi mungaizenge bwanji?
Mzimayi akuyenela kukakhalaso ku prison pa mulandu wakupha mamuna yemweyo? Kapena adamaliza kale sentence?

17/07/2025

Happy follow-versary to my awesome followers. Thanks for all of your support! Tchaka David

16/07/2025

Big shout-out to my newest top fans! Roselyn Nkhoma, Caro Kafumbwe

Say something πŸ₯°
25/05/2025

Say something πŸ₯°

Chifukwa chimene President wa ku Burkina Faso wapangira Bun ma video ndi ma website olaula dziko mwake Tsopano President...
22/05/2025

Chifukwa chimene President wa ku Burkina Faso wapangira Bun ma video ndi ma website olaula dziko mwake

Tsopano President Ibrahim Traore officially walengeza kuti Wapanga Bun ma porrrrn videos and websites dziko lawo la Burkina Faso

Komanso funso mkumati
Kodi anthu a ku Burkina Faso akuti chani zakubanidwa kwa ma website olaula Dziko mwawo?

Izi zikutanthauza kuti ma citizen a ku Burkina Faso sazitha kapena kuti sizimatheka kupanga search ma website kuti aonere ma video akusaweruzika

Malingana ndi Ibrahim Traore akuti wapanga izi chifukwa choti ma website ndi ma videos akusaweruzika aja amasokoneza achinyamata kaganizidwe kazinthu mu zinthu zosiyanasiyana komanso zifukwa zazikulu kwambiri zimene wapangira decision imeneyi waulura ndi iziπŸ‘‡

ANTHU PENA ALIBE CHIKONDI AMATAπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚.Mu mwezi wa May ,m'chaka cha 2018, oimba wa m'dziko la America  ali pachithunzi  m'mu...
20/05/2025

ANTHU PENA ALIBE CHIKONDI AMATAπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚.

Mu mwezi wa May ,m'chaka cha 2018, oimba wa m'dziko la America ali pachithunzi m'munsiyu otchedwa Lao 6ix9ine , ankaimba pa stage live show ,ndiye ali m'kati mopanga perform mu club yomwe ankaimbayo anapanga chiganizo choti ati awone m'mene ma fans ake amamukondera mu mdzinda wa New York komwe ankaimbako ndipo anadumpha m'mwamba ndikuzigwetsera kuchigulu cha anthu omwe anali mu show ija , muja amapangira ma celebrity, ati ndicholinga choti anthu amuwakhe. Koma atangoziponya anthu aja anasunthira mbuyo ndikumupasa malo okwanira ndipo anagwela pa concrete ,pompo kukomoka ndipo show inathera pompo.

Ibrahim Traore Mkazi wakale wa President wa dziko la South Africa a Dlamin Zuma lero adakayendera a Ibrahim Traore, Pres...
19/05/2025

Ibrahim Traore

Mkazi wakale wa President wa dziko la South Africa a Dlamin Zuma lero adakayendera a Ibrahim Traore, President wa dziko la Burkina Faso atamva za mbiri yake yotukula dziko lake mwachangu kwambiri.

A Zuma agoma kuona zitukuko zikuvumba ngati madzi ochokera ku mwamba.

Ibrahim Traore wagometsa angakhale azungu.

Mbambande!

Here we go again with Apples  delicious πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ₯°πŸ₯°
19/05/2025

Here we go again with Apples delicious πŸ˜‹πŸ˜‹πŸ₯°πŸ₯°

Address

120 Plain Street
Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Issac super love story posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Issac super love story:

Share