30/10/2025
Anthu olusa omwe akupanga mademo ku Tanzania awophseza kuti akukatentha nyumba ya oimba Diamond Platnumz.
Anthu omwe akupanga ziwonetsero zokhuza zisankho ku Tanzania panopa awotcha shop yogulitsa zida za electronics ya oimba uja Juma Jux uja anapanga collabo ya nyimbo za Enjoy komanso Ololufemi ndi Diamond Platnumz, komanso anthuwo awotchanso shop yogulitsa ma electronics ya oimba Billnass ati chifukwa oimbawa akusapota president wa dzikolo Mama Samia Hassan.
Oimba ena monga Diamond , Harmonize,Rayvanny ,Alikiba akhalanso akusapota chipani cholamula cha CCM ndipo anthu akuti oimbawa awakhumudwitsa pololera kuwataya anthu nkumasapota zinthu zosakhala bwino.Lero anthu awophseza kuti akukaotcha Wasafi records studio ,Wasafi Tv and Radio komanso nyumba ya oimba Diamond Platnumz.
Diamond Platnumz naye walemba izi pa masamba ake a mchezoππππ
βοΈ
Dear my Mama President Samia Suluhu Hassan,
You are a great leader who works hard and makes wise decisions. Sometimes people don't appreciate leaders until they're gone, but we see the good things you've done for Tanzania.
You've improved education, health, agriculture, fisheries, infrastructure, and more. We know it's not always easy, and some people might criticize you, but don't let that discourage you. Even important people in history faced opposition.
There are many Tanzanians who support and appreciate you. We'll show our support by voting for you tomorrow. I and the institutions I lead will vote for you and Dr. Nchimbi to keep working towards a better Tanzania.
Wishing you a good night and best wishes for tomorrow's elections.
Ukuku the whole Wasafi crew is under CCM political party ,even wa manager wa Diamond , Babu Tale is the MP under CCM. Wangotsala Diamond -yu music ikalowa pansi adzaimiranso U MP. Ku Tanzania kulibe ufulu weniweni anthu amawopa, it's only panopa ayankhulapo kupanga ma demo koma siziphula kanthu.πππππ.