Nkhwinimba Online

Nkhwinimba Online Arts and entertainment
(3)

Prophet Habakkuk naye Ali pa kamuzu Stadium kuzawona mmene ntchito ikuyendera😂
03/10/2025

Prophet Habakkuk naye Ali pa kamuzu Stadium kuzawona mmene ntchito ikuyendera😂

Kumanjako ndi mayina anyamata kuchokera ku Congress omwe alowa ku MBC dzanadzanali esh.
03/10/2025

Kumanjako ndi mayina anyamata kuchokera ku Congress omwe alowa ku MBC dzanadzanali esh.

Kalibu guys.
03/10/2025

Kalibu guys.

Nkhani yachisoni 💔😭A nduna akale aza chuma a Ken Lipenga  alengeza zakumwalira kwa mwana wawo Enuku Lipenga (ali kumanze...
03/10/2025

Nkhani yachisoni 💔😭

A nduna akale aza chuma a Ken Lipenga alengeza zakumwalira kwa mwana wawo Enuku Lipenga (ali kumanzereyo) kutsatira ngozi ya galimoto yomwe anapanga...

Mzimu wake uwuse mu mtendere 🕊️🕊️

03/10/2025

News In

Counsel Oscar Taulo wa congresss wathamangitsidwa pa kamuzu Stadium pomwe anabwera kuti alowe DPP.

DPP ya ulendo sikunyengelera💪

03/10/2025

Kondwani Kachamba Ngwira wafika pa malawi 💪

News InAfter dining with the incompetent MCP regime, Tay Grin makes a U-turn. He now wants to align with the Great Retur...
03/10/2025

News In

After dining with the incompetent MCP regime, Tay Grin makes a U-turn. He now wants to align with the Great Return of Proven Leadership.

Komano anali kuti kuti angofikira ku inauguration?

03/10/2025

News In:

Mmodzi mwa anyamata a MCP omwe anakatchola ku Limbe Cathedral wagwidwa ndipo pakadali pano ali ku police.

Dziko limachepa ili ulamuliro ukasintha.

03/10/2025

Anthu aku Dowa m***a kubwela nawo kolumbilitsa president sikuti tikuletsa. Koma maheu aulele kuno kulibe🤣

Tisayiwale izi
03/10/2025

Tisayiwale izi

03/10/2025

Attention:

Mawa osalola munthu wa chilendo kuwandikira adad pa kamuzu Stadium

03/10/2025

Mangochi sakuchezatu

Address

Johannesburg
46614

Telephone

+27724745081

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhwinimba Online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nkhwinimba Online:

Share