01/09/2026
Mlandu Uwu ineyo Ndikhoza kuwina straight 🤞
Mai ake amwana uyuyu ndiachitsiru, bwanji samakanena ku Police nthawi imene mwana wawo anali ndimimba?
Panopo aganiza zokamusumira munthu pomwe mwana wabadwa? Anali kt nthawi imene mwana wawoyo amafika pimajambulitsa zithunz, anali kt nthawi imene mwana wawo anali ndimimba?
Zkuoneka kt Mai ake a mwanayu nawoso ndi Hule amapanga Busnes pa mwanayu nkhani imeneyo iloweso mu Court Ndipo ndadzipeleka kukamuimilira oganizilidwayo mwaulele
ABoma ndiloleni kukhala ndi Linces ya Zaka TV Channel kt anthu ena tidziwauza zoona