Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV Not impersonating, this is Bakili Muluzi TV Fanz Page 🔥🙌

13/09/2025

No fuel
No electricity
No forex
No sugar
No cement
No paraffin
Mavuto osayamba china chani ???

13/09/2025

Ndi wandale uti amene vote yanu atayimvere fungo lachiwiri li?

"YAFIKA YOKHA WEEKEND | Pali 20,000MWK iyi, anthu 4 omwe comment yawo sikhala ndi LIKE! kufika 7 o'clock madzuro, aliyen...
13/09/2025

"YAFIKA YOKHA WEEKEND | Pali 20,000MWK iyi, anthu 4 omwe comment yawo sikhala ndi LIKE! kufika 7 o'clock madzuro, aliyense TRANS I'D ya 5000MWK (each)

4 OWINAWO APOSTEDWA PAMUDZI PANO!

Big shout out to my newest top fans! Ngwazi RB, Simon Kasalu
10/09/2025

Big shout out to my newest top fans! Ngwazi RB, Simon Kasalu

10/09/2025



Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) lati mchitidwe omwe ena akuchita pogawana zotsatira za ophunzira omwe analemba mayeso a MANEB pamasamba a mchezo opanda chilorezo ndi zosavomerezeka.

Kalata yomwe mkulu wa MACRA a Daud Suleman asainila yati kutero ndi kulakwira lamulo la mchaka cha 2024 lokhudza chitetezo chamauthenga otetezedwa kuphatikizapo zotsatira za mayesowa.

Iwo achenjeza kuti kupezeka olakwa pa mlandu ogawana zotsatirazi umapereka chindapusa komanso kumangidwa kumene molingana ndi lamuloli.

Wolemba: anonymous

10/09/2025

Magulagula ena anapeza nazo mamina mu thobwa 🙄🚶 Good morning 🌞

Tamia ja   🤣🙌
09/09/2025

Tamia ja 🤣🙌

09/09/2025

Mwathira kale mbali ya kumeneko?

08/09/2025

Ace Jizzy & Ching'aning'ani nkhondo iyiyi sitha bwino ndithu 🤣🙌

08/09/2025

Mavuvu Media

Address

Pretoria East

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bakili Muluzi TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share