
25/09/2025
*_TIDZIWE ZA MIMBA
(PREGNANCY).
⏩ The union of an egg and s***m is called fertilization, after fertilization done mimba imayambika pamenepo.
⏩ Mimba imatha k*tha 40 weeks or just over 9 months kuchokera tsiku lomwe mudasiya kusamba nde pali ma stages amimba komanso ma types ake ndi zina zambiri zomwe ndizifotokoze pano.
⏩ Mimba imapanga involve nkhani zambiri zomwenso ziri very sensitive chifukwa attention yonse ya couple and relatives imakhara ili pomwepo kudikikira kulandira mphantso yapadeladera so I'll try to be much attentive pa ma areas okhawo omwe tikambirane pa lesson ino.
↘️ ZIZINDIKILO ZAKE
↪️ Chizindikiro chachikuru cha mimba ndicho kusiya kupanga menstrual period ( Nsambo ).
↪️ Then pansi pa mchombo pamadzatuluka nzera wakuda ( blue vein) komanso chilakolako chogonana chimachuluka.
↪️ Dzotsatira zosiya kusamba mabere amakungana kapena kusongoka ( Kupereka chikoka ).
↪️ Umachita nseru pafupipafupi pena mpaka umasanza ndipo umayamba kusara dzakudya zina.
↪️ Nkazi amene ali ndi mimba amakodza pafupipafupi komanso amadya kwambiri maka za tswayitswayi.
↪️ Amanva k*topa komanso amakhara ofooka kwambiri ( fatigue ) phuma kapena k*ti befu akangogwira ntchito pang'ono.
↪️ Morning sickness, kungodzuka mmawa ndi ma mood osadziwika bwino.
↪️ Kunva kuwawa mutu komanso body temperature imakwera enanso amava kuwawa nsana.
↘️ KUYEZA KWAKE
↪️ Tengan Colgate wa white ikan mu kabotolo koonekera nde mukozelemo mikozo ya mmamawa ikhale 5hrs onan ngati maonenedwe akusintha kusanduka obiliwila ndek*ti ndi mimba.
↪️ Pezani ka piece ka anyezi ndikulowesa kumaliseche kwa suspect yo kagone konko nde kumapanga absorb ma onion properties kupititsa mmagazi then mawa podzuka mukalankhulana naye mukazamva fungo la anyezi ndek*ti ali ndi mimba.
↪️ Njira ina njoti muyike ma spoon atatu a brown sugar mu botolo nkukodzelamo nkozo wa mammawa ngati suga uja akupanga thovu ndek*ti mwaima.