UYEEH TV

UYEEH TV BREAKING NEWS๐Ÿ“ฐ ๐ŸŒ
INTERTAINMENT PROGRAMโœจ๐ŸŒŸ๐ŸŒ

23/08/2026
28/07/2026

Cheche kule

26/07/2026

๏ฟฝ

Mai Yankho Luka omwe amakhala ku Blantyre atengera chipatala Cha Mulanje Mission ku court kamba kowachotsa chibelekelo z...
19/07/2026

Mai Yankho Luka omwe amakhala ku Blantyre atengera chipatala Cha Mulanje Mission ku court kamba kowachotsa chibelekelo zomwe zinachitika chifukwa chakulekelera kwa ogwira ntchito a pa chipatalacho.

Mu November chaka cha 2023, Mai Luka anabeleka pa chipatala Cha Mulanje Mission panjira ya Caesar. Omwe anawabeleketsa ndi Dr. Smart mothandizana ndi ma medical officer ena.

M'modzi mwa ma nurse omwe anamusiya kuti amalizitse kuwasoka a Mai wa, Linda Ekhama, anapezeka wayiwala thonje muchibelekelo.

Ndiye Mai wa atapangidwa discharge pa 4 November, 2023, basi tu amangodabwa kuti m'mimba mukuwawa komanso amangopanga period yomwe imatulutsa zonunkha kwambiri.

Atabwelera ku Chipatala ko anakapeza mistake imeneyi komanso anakapeza kuti chibelekelo chawonongeka ndipo njira yokhayo yowathandizila ndi kuchotsa basi.

Ndipo anachotsa.

Mai Yankho Luka anakadandaula nkhani yi ku Medical Council of Malawi komwe anangomuzuzula nurse, Linda Ekhama, kuti zomwe anachita zinali "gross medical incompetency" koma chipatalacho sanachipeze cholakwa.

Ndiye apapa Mai Yankho akufuna chipukuta misozi popeza kulekelera wa ogwira ntchito kunawaluzitsa uterus wawo

Copy:

14/07/2026

๏ฟฝ๏ฟฝ๏ฟฝ๏ฟฝ๏ฟฝ๏ฟฝ

11/07/2026
10/07/2026

ANTHU MULI ND CHIPONGWE
๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€
๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

06/07/2026

04/07/2026

๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ˜€๐Ÿ˜€๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Address

SOUTH AFRICA
Pretoria

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UYEEH TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category