A matope

A matope A matope content creator/story writerπŸ“Œ





follow amatope πŸ“ŒπŸ”₯

14/06/2026

Part 1 ya the boy chidole chamoyo πŸ™ŒπŸ”₯

πŸ˜­πŸ’” ZACHISONI KWAMBIRI!Mwana wa ku Zimbabwe yemwe ankadziwika pa social media ngati "My Manager" wamwalira mwadzidzidzi. ...
14/06/2026

πŸ˜­πŸ’” ZACHISONI KWAMBIRI!

Mwana wa ku Zimbabwe yemwe ankadziwika pa social media ngati "My Manager" wamwalira mwadzidzidzi. Malinga ndi malipoti, akuti wamira m'madzi. πŸ˜­πŸ’”

Mwanayu, wobadwa mu 2023, ankakondedwa ndi anthu ambiri chifukwa cha ma content omwe amapanga ndi bambo ake.

πŸ•ŠοΈ Rest in Peace, Manager. Gone too soon. πŸ’”πŸ˜­

πŸ•ŠοΈπŸ’”

MA BACA SIMUYAKHULA BWINO πŸ”₯πŸ”΅πŸ”΄ Sorry, ife timamukonda Rashford, koma zoti tipereke €30 miliyoni? Ayi, mukafune club ina.M...
13/06/2026

MA BACA SIMUYAKHULA BWINO

πŸ”₯πŸ”΅πŸ”΄ Sorry, ife timamukonda Rashford, koma zoti tipereke €30 miliyoni? Ayi, mukafune club ina.

Mukuti Rashford watha, ndiye bwanji mukukakamiza kuti Barcelona imulipire ndalama zambiri chonchi? πŸ€·β€β™‚οΈ

Komanso, a Manchester United muzidziwa kusiyana kwa ma size. Ngakhale Barcelona itasiya kusewera mpira kwa zaka 100, mbiri yake simungayifike mosavuta. πŸ˜ŒπŸ†

Ndipo chowonadi n’chakuti si Barcelona yomwe ikupempha Rashford. Inuyo ndi Rashford wanuyo ndi amene mukufuna kubwera ku Camp Nou. Ife timatha mpira popanda iye. πŸ”΅πŸ”΄

Player akabwera ku Barcelona amapeza mwayi wokhalanso pa mlingo wapamwamba wa mpira wapadziko lonse. Nanga tikalipirenso €30 miliyoni? πŸ˜…

Ngati simukufuna kugulitsa pamtengo womwe ukugwirizana ndi msika, mugulitseni kwina. Ife tilibe vuto. πŸ’™β€οΈ

πŸ”΅πŸ”΄πŸ”₯

πŸ™†β€β™€οΈπŸ‘‡πŸ‡ΏπŸ‡¦ NGATI LAMULO ILI LINGAYAMBE KUGWIRA NTCHITO APA, NDE TITHA BAS!Dziko la South Africa lakhazikitsa lamulo lolanga...
12/06/2026

πŸ™†β€β™€οΈπŸ‘‡πŸ‡ΏπŸ‡¦ NGATI LAMULO ILI LINGAYAMBE KUGWIRA NTCHITO APA, NDE TITHA BAS!

Dziko la South Africa lakhazikitsa lamulo lolanga anthu omwe amalemba ntchito obwera ochokera kunja osakhala ndi mapepala ovomerezeka. Anthu opezeka olakwa akhoza kulipira ndalama zambiri kapena kukumana ndi chilango cha ndende.

Kodi inu mukulandira bwanji nkhaniyi? Kodi ndi njira yabwino yotetezera ntchito za nzika za dzikolo, kapena ikhoza kubweretsa mavuto ena?

Tiuzeni maganizo anu m'ma comments. πŸ‘‡

πŸ˜­πŸ’” ZOMVETSA CHISONI!Mnyamata wina yemwe amadziwika kuti Hope, yemwe adagwirapo ntchito pa Chipatala cha Kauma, wamwalira...
12/06/2026

πŸ˜­πŸ’” ZOMVETSA CHISONI!

Mnyamata wina yemwe amadziwika kuti Hope, yemwe adagwirapo ntchito pa Chipatala cha Kauma, wamwalira ataphedwa ndi anthu osadziwika ku Kauma, Lilongwe. πŸ˜­πŸ’”

πŸ•ŠοΈ Rest in Peace, Hope. Chitonthozo ku banja, abale ndi anzake pa nthawi yovutayi.

12/06/2026

Nthawi zambili yemwe umamukonda siyemwe amakukonda πŸ™Œ

12/06/2026

Eshiii mwandipanga chipongwe

09/06/2026

Palibe chosatheka πŸ™Œ

07/06/2026

Dolo kangapo πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

AMANGIDWA KAMBA KODULA ZALA ZITATUApolisi ku Monkey Bay amanga Mavuto Saulos (66) pomuganizira kuti anadula zala zitatu ...
07/06/2026

AMANGIDWA KAMBA KODULA ZALA ZITATU

Apolisi ku Monkey Bay amanga Mavuto Saulos (66) pomuganizira kuti anadula zala zitatu za Chikondi Samuel chifukwa chomuganizira kuti anaba mbatata.

Chikondi akulandira chithandizo kuchipatala, pomwe Mavuto akuyembekezeka kuyankha mlandu wovulaza munthu.

Kodi mukuganiza bwanji pa nkhaniyi? πŸ‘‡πŸΎπŸ’¬

πŸ“Œ Follow page yathu for more news updates.

Address

67
Pretoria
15

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A matope posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share